Email a copy of 'MCP MPs conspire to unseat Jumbe as chair of agriculture committee ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP MPs conspire to unseat Jumbe as chair of agriculture committee ' to a friend
Chief cashgate suspect and businessman, Oswald Lutepo, does not cease to amaze. On Friday, November 21, he spoke to Zodiak...
Ndemanga zina mukamalemba kumaganiza kaye, ndiye poti Alomwe’nu nkhani ya sukulu ndi apongozi, n’chifukwa chake mukumangolemba ndemanga zopusa zokhazokha. MCP ngati analephela a “tcheya” kuyithetsa ndi ndale zao zozikonda, m’malo mwake chipani chawo ndichomwe chidang’ambika ngati makatani. Inu pangani zanu zomangochindana n’kumaswana ngati nkhumba.
President weniweni wa chipanichi ndi Jumbe aliyense akudziwa .Ndiye apa ndi nkhani yoti Jumbe achoke mu MCP ngati Dadza kuti makanja akamalankhula nkhani yake ya njee!! ya fedral asowe omutsutsa.Ndi congeresi imeyi sizasintha olo pang’ono. Ife alomwe ndiye tidathana nayo kale. Ife ndi chala mwamba basi,zikavutitsitsa ndi ung’onoung’ono.
Abale mwatani nokha nokha a banja limodzi, musiyeni Jumbe alibe chifukwa.
Kodi nkhamizi ndizolimbirana maudindo eti? Timangomva feadalism, seasation, etecetc. komatu MCP ikuoneka kuti ndiyopheka kusokonezedwa. Nanga anayamba si amai kumpatsa dollar Lutepo kuti akasokoneze konvention. Lutepo watiuza kale. Ufumu ngati uukirana siungalimbe. Abusa akudziwa zimenezo. Kodi MCP are you such greedy?
Abambo Jumbe, ichi ndi chiyambi chabe. Chipongwe chimwene munamuchita mkazi wanu wakale uja chidzakutsatani moyo wanu onse. Kodi simunkanamiza anthu dziko lonse la Malawi mmene munkachita kampeni ya u prezident wa MCP kuti ndinu katswiri wa “Wealth Creation” chonsecho mpaka pano mukukhalabe nyumba ya rent ku Area 47. Kodi 100 hectares za mtedza zija simunagulitsebe kuti mwina mungaguleko nyumba ku mchesi? You have a problem. You talk too much. And you think you know everything kuposa wina aliyense. Zomwe akunena akomiti ya Agriculturewo ndi zabodza? kodi akukunamizilani? zonse zomwe alemba ndi zoona. Mumadzimva kwambiri. Vuto lanu mamakonda atola nkhani kwambiri.… Read more »
Pamene pali nzeru pamakhala kutsutsana. But at the end there is a thing to agree upon.
Jumbe ninkholokolo ndipo azizake amutulukila. antha ngati makatani. there is no way he can unseat CHAKWERA, no matter what ways he can use. azingodya ndalama akumupatsazo, at the end of it adzayaluka yekha. MCP ITS MCP. THE MOTHER N FOUNDER OF POLITICS.
OH OH NANUNSO MCP BWANJINSO.
Someone having the named qualities,does not qualify to be an mcp member,however jumbe must be very unfortunate,watch out jumbe!
Ameneyo ndiye Felix ndimadziwa ine. Simwana ndiwankulu amene akulimbana naye atha ndithu. Bwanji Jessie sakutsekula milomo yake akumudziwa.