Email a copy of 'MCP MPs rebuffs Mutharika’s banquet: ‘Mapwevupwevu govt’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP MPs rebuffs Mutharika’s banquet: ‘Mapwevupwevu govt’' to a friend
Government has gone ahead to sale the wholly State-owned Malawi Savings Bank (MSB) after posting a pre-tax profit of K2.5...
Maliro akatuluka mnyumba, samabwerelanso. DPP inafa kale koma nomweno ma Civil Servants inuyo. These problems are of ur own making.
its sad that our leaders don’t know what to priotise. this is all due to greed and selfishness. I sympathise with civil servants, but you are just seated phwiii waiting for Mtambo, Mayaya and Kapito to fight for you. Wake up, the ball is in your court!
I am commenting this today this year 2019. God is not a man to play with. Inu a MCP Mukuzitumbwa pano kudzera mu Nyasatime. Tsiku lizabwera mudzalowatso mu boma lizakulakani ili. Anthu amene akukuyamikilani pano ndi amene azizakunyozanisnoni. A Malawi azerezeka ndi umphawi sakudziwa chimene akufuna. Believe me or not. Mwagundika ndikunyoza apa ngati zenizeni.
Kkkkkkkkkk fund raising ya mowa ndi nsima done by ahead of state no no peter thus apit.Mr peter go a round the global like jb.I credit her within two years she did something’s,you 2yrs nothing wamuna kumangopanga kitchen topup
Kamulepo MAPWEVUPWEVU NDIYE KUTI CHIYANI ,KOMADI BOMA ILI NDIYE NDILAUSILU
MCP a bunch of sorry losers, still licking your loss up to today, would you grow up? Come on!
NA BOMA ILI, NTCHITO YILIPO. CHIUTA TOVWILANI. NDISE WANTHU WAKUTONDEKA. TIKUTONDEKA KUPULIKIRA WANYITHU PALA WAKUTISOKA. MIZIMU YIHENI NDIYO YAKULA. TAWIKA KUJITEMWA PA NTHAZI NA KULUWA WANYITHU. FUMU LONGOZGANI CHARO CHITHU. PALA AWO WALIPO PA MIPANDO WAKUTONDEKA, IMWE, FUMU MUNGAMANYA WAO WANGATOVWIRA. THANK YOU LORD, FOR ANSWERING THIS PRAYER. AMEN.
Palibe chaphindu chilichonse chomwe mcp inganene. Ikhala ku oppozishoni konko mpaka 2050 kkkkkk chipani chankhalamba ndi anthu aphuma ndi kufuna kulamula kkkkkkk mpofunika tichiunike bwino chipani chimenechi, chisinthe dzina. mbava za anthu. chipani chapakati kkkkk. ati amedza sidik mia kuti akhazikitse mcp kumwera shiiii longa mbuya.. step 1 Sidik sponsoring Peter Simbi to take over leadership of mcp in the whole southern region. Step 2. Sidik Mia vying for running mate of MCP in 2019 . Step 3 Chakwera planned for removal during MCP Convention. Step 4 Msonthi takes over leadership.
Failed government. Pay us our salary, Mr. Peter Muntharika with the K92B which you, your family and those of Muralkho Wa Lomwe people stole from us, poor Malawians.
Even myself I can support what DPP is doing!