Email a copy of 'MCP, PP against naming stadium after Bingu' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

221 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Katswiri wa Ndale
Katswiri wa Ndale
9 years ago

Kumamvesesa bwino nkhani musanakomente anyani inu, moti ankhutukumve inu mwamvapo zoti akukana dzina la Bingulo, zikungofunika kumawapanga consult a Malawi potchula dzina osati mwawokha ayi.

BOX 13 BILILA, N U
9 years ago

Just useless noise,what if we call it Joyce Banda stadium,does it make sense?Bingu initiated it,why not muluzi snr? Bingu had clourful dreams,if u argue go read his book,African dreams from poverty to prosperity,then u will known Bingu wamutharika big man,not bigmouth kabwira msonda,short sighted. Shut up,know when to speak.

Ajuju
Ajuju
9 years ago

That is a great achievement, by giving example to upcoming leaders, congratulations

Phirilamatiya
9 years ago

But you know, this will encourage the next leaders to facilitate big projects in order to be named after them. I know Chakwera will do more than this in the next term. There is no case in this matter. But Malawians should always be consulted. Ana a kutsogolo azizdziwa mizwanya ya ma president amene anapanga zakupsya.

Tryness Gondwe
Tryness Gondwe
9 years ago

Amalawi nkhani ya ndale tizipasana po ulemu apa. A MCP mulibe manyazi munazunza anthu muno ndipo ineyo amalawi kuzangochita Tsoka kuti anthu awa akuphani atenga boma izakhala mistake yoopsa. Anthu oipa awa ife abale athu anachoka muno chifukwa cha nkhaza za MCP. Ma cousin athu up to now amakana kuzaponda ku Mw chifukwa cha anthu oipa a jealous. Inu amene Muli ana muziwafusa bwino makolo anu za chipani chimenechi. It is a big shame kuti achinyamata ena osamba bwinobwino amakakamira MCP ati chifukwa makolo awo ndi or anali a MCP or anapanga benefit ndalama za makadi. Mumangosobyeza umbuli to associate… Read more »

kalumo
kalumo
9 years ago

Imeneyi ikhale John Chilembwe national stadium osati bingu ayi . cabinet yaku Malawi singatsutse zimenezi chifukwa aliyense amapembedza unduna kuti usathe.

Azakhali
9 years ago

even if u go and ask ZBS already asked ppo’s views majority chosed de late Bingu,it its not asurprise just bcoz Bingu ws de one who initiated de devpment osamangosusa bcoz ndinu a opposition mwamva akanyapwa inu?

Abiti
9 years ago

Asafune akhale it will b BINGU NATIONITIONAL STADIUM in area 48,LL.

Ajijo Mapwiyamunlupali
Ajijo Mapwiyamunlupali
9 years ago

Ntchito za president aliyense zizimuchitira umboni. Dzinalo likhale lomwelo!

Wanga ndi yemweyo
Wanga ndi yemweyo
9 years ago

I think we Malawians like arguments. Where there is no cause for arguments, we deliberately create one. One sure way of doing this is to name national assets after political figures. Why can’t we give such structures any one of the thousands of neutral names around? Cholinga? Kuti timve enawo anena chiyani, si choncho? Then when another political party comes to power, the name will be changed to that of another expired political figure. The problem is that in Malawi, the country belongs to politicians, especially the ruling party of the day. The rest of us are simply luggage carried… Read more »

Read previous post:
Man pleads guilty for attacking Malawi President’s portrait: “I am suffering’

A 37-year-old Aaron Mbengo from Samilani Village in Traditional Authority’s Chilipa area in Balaka pleaded guilty  to attacking a portrait of...

Close