Email a copy of 'MCP, PP split in Blantyre rallies: Opposition demands police protection' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

8 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mzozodo
Mzozodo
8 years ago

I thought you say Malawi is a religious country? How come a lot of the comments I read on Nyasatimes show that there are alot of Southerners who worship Mutharika and his DPP? I thought you say there is no other God than God?

chaz.com observer mission
chaz.com observer mission
8 years ago

Amalawi ndife fuko limodzi.
Polankhulana tiziganiza ngati fuko.
Kumozambiki mavuto anayamba ndi kulankhula kwa msontho ngati momwe enanu mukuchitira.
Kukanakhala bwino kuti enanu mukanapanda kubadwa – chifukwa mukuipitsa mbiri ya fuko ladziko lino

Mbuzi
Mbuzi
8 years ago

Ndinthawi yachitukuko osati campaign. Chakwera waufunitsitsa udindo. A Jersey politics si ma theory kapena philosophy yamkalasi. Munalakwa kupita kwa pastor Mboro

TSAMBALIKAGWA
8 years ago

Iwe Ngwenyama Ngwenyama, Kodi Chipani cha MCP, Chinapha Amako? Anthu onse akumwalira tsiku ndi tsikuwa akufa chifukwa cha MCP? Kodi Matafale anaphedwa ndi MCP? Robert Chasowa anaphedwa ndi MCP? Anthu 22 paziwonetsero zija anaphedwa ndi MCP? Kodi Magazi ali ndi chipani cha MCP amachokera kuti? Yemwe ali ndi Umboni kuti MCP inapha Amake kapena Atate wake, Otsibweni ngakhale Chemwali kumene ayenera apite ku Police kukapeleka dandaulo lake Koma ngati ndiumbuli ndiye ndibwino kungokhala chete.

Zidura Ntengo UndigwereA
Zidura Ntengo UndigwereA
8 years ago

1. Holding separate rallies on the same day, in the same city, just shows MCP and PP are up to no good. And they are out to undermine the Police; and the Police know it! MPS is an organization made up of people; people with feelings too. I do not understand MCP and PP’s thinking on this? Rationale, any one? Is this an attempt to pad their numbers, so that the organizers can hoodwink us: by adding X and Y from the two rallies, the total would actually SEEM more than Z as would have been at a single combined… Read more »

Phwisa
8 years ago

Kabwila’ s blame of police goes beyond Mzuzu fracas. Since the Chancellor College education saga and her arrest on treason case Kabwila vowed to demean the police authority. PP and MCP will never work together. There are in fightings in MCP and PP with Kabwila promoting a faction to oust Chakwera but pushing this on DPP. Ati ndale a Kabwila

Ngwenyama Ngwenyama
Ngwenyama Ngwenyama
8 years ago

A PP mwachita bwino kusiyana ndi chipani cha
magazi mmanja. Pitilizani kutsata democracy imene a mayi Joyce Banda amadziwika nayo ndipo
ndikukhulupilira kuti anthu okutsatirani adzakhala okondwera. Inu a PP mumadziwika ndi
ulamuliro wabwino pomwe a Kongelesi amadziwikanso ndi nkhanza zawo kupha anthu powaponya ku n’gona, kumanga anthu Nyakula, kukakamiza anthu makadi kuphatikizapo mwana ali mmimba ndi zambiri.
A PP dziwani kuti a Kongelesi ukufuna kukugwilitsani ntchito kuti alowe mmboma mwa chinyengo. Ubwino wanu a Malawia akuudziwa ndipo adzakuvoterani pa nokha. ntchito zabwino za a Joyce Banda aliyense akuzidziwa.

Joseph Banda
Joseph Banda
8 years ago

Jessie Kabwila, Blantyre is a civilized districts, you cannot see what happened in the Mzuzu -NORTH. Otherwise Msonda should have been beaten.

Read previous post:
Angry mob beat suspect to death in Balaka

Reports of mob justice are refusing to die in the country with a recent incident about unknown man beaten to death in Balaka district...

Close