Email a copy of 'MCP 'rebel' leader Chatinkha claims getting death threats' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Hatton Mbewe
Hatton Mbewe
7 years ago

A Chatinkha, musavutike ndi kufufuza. Amene akufuna kukuphani ndi omwe anapha a Gadama, a Matenje, a Sangala ndi a Chiwanga.
anthu akuphawa, ndi oipa mtima regardless of their church background.

DOBO
DOBO
7 years ago

Chokha chongobwera pa MBC,zonse zidaonogeka pa umoyo wandale.Mwina kapena mungoyesa DPP yomweyo.

Kanyauzi
Kanyauzi
7 years ago

Chatinkha, wadya zambiri za DPP koma walephera kukwaniritsa zomwe anakutuma a DPP and no they will be on your neck so that you pay back their money. They are the ones giving you death threats. DPP imapha mayi, ukapanda kuwabezera zawo akuchinda ndi Mpeni ma Cadet a DPP. Udaziyamba wekha ndipo uyembekezere kuchindidwa ndi mipeni ndi zikwanje.

sazilala mbuno
sazilala mbuno
7 years ago

koma ndr kusakwanitsidwa, kwa AMERICA munakhala mwa ofuofu under our parents tax. osangoleka bwanji muti muphe azimuna a eni ake ndi matanda. decades and decades mukudya za boma . greedy pipo.

mahope a Seodi
mahope a Seodi
7 years ago

koamatu sibwino. msiyeni mzimayi. mukamatero ndiye kuti wakukanani kuti mumuchinde basi muthane naye politically azibambo muli ndikanthu. Jessie anakana kumuchinda basi munamuchotsa.uyunso chimodzimodzi. women empowerment yakanika basi

Funsirani
7 years ago

mmmmm amayi awa ndi kathyali, dyera komanso ndi madzi amene satha kupanga chiganizo paokh,amangolondola kumene kwaloza khwawa.

dee Kay
dee Kay
7 years ago

Death threats is not the hallmark of MCP but the same DPP whom she is helping. Yalephereka deal wakanika kupanga ganyu ndiye basitu zakuvuta. Ulipira bwanji ma million anakupatsa aja?

Yahya Jammeh
7 years ago

Chatuinkha is saying that as a pretext to find a way of returning to the MCP fold because she has realised that she was fooled by the thieves. Mlongo, just follow the footsteps of Mulomo otherwise if you continue aligning yourself with the thieves, you will never achieve your political ambition, they will just use you like Nakoma . This is free advise. I will rule Gambia for a billion years.

Thyolo Thava
Thyolo Thava
7 years ago

Madets amzake ndiapemene akumuopyeza. Wadya zambiri za DPP. Simunagwane moyenela.

Game_Changer
Game_Changer
7 years ago

I support Chatinkha’s game changing attitude, this woman has class, aptitude and ability to think outside the box, She is not your ordinary person. You go where mos tof us dont dare! YOLO! ( You only live Once! ) And you have chosen to make the most of it!

Read previous post:
Malawi face K8mil fine and ban over Africa Cup of Nations withdrawal

Malawi is likely to face financial penalties of up to K8 million for pulling out of the 2019 Africa Cup...

Close