Email a copy of 'MCP replaces parliamentary candidate who died in car crash' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP replaces parliamentary candidate who died in car crash' to a friend
Malawi Police Service in Mzuzu have arrested a 42 year old woman identified as Joyce Mkamanga for allegedly burning legs...
A better word would have been deceased than dead parliamentary candidate, lets be a little sensitive
Your name should have been Cardiac Arrest and not Heart attack , let’s be a little sensitive…
KKKKKKKKKKKK
Guys, your comments are very unfortunate. How dare you say wajudula msanga.
On the other hand, you nyasatimes need to check your selection of words. You should have said, MCP replaces the departed Chikwawa Central 2019 aspirant.
kkkkkkkkkkk !!!! mcp siinasiyebe zophana zija ?
Inu nde mukhala nchonco…muzindikira mwatsala nokha
Olosela analosera kale….MCP 2019 Boma
Don’t be foolish. Some lost a loved one. It was a terrible car accident.
Kkkkkk…inu mukungotaya nthawi…mmene zinthu zilili pano ..zikuchita kuwonekelatu….ndipo olosela analosera kale…. MCP 2019 BOMA
Iwe psuta dpp idatha ingotseka pakamwa pako
MCP YAKALE YOMWE IMAPHA ANTHU NDIYOMWE MNALI ACHINA DAUSI, NTABA.
koma sanamujudule mzakeyo ameneyu?
gyz please avoid mau olakwika pano. kufa ndi kufa iyi inali ngozi yoopsa zedi .mzimu uuse mumtendele
Maganizo anu. Please have mannas anzanu anataya okondedwa wawo. Chonde your comments should be reasonable
Inu mukamayankhula zonyansa pa imfa ya Bingu ndikumaganizanso kuti Peter afa chimodzimodzi, mukuona ngati anthuwa alibe okondedwa awo? Bvomerezani kuti mwamujudula munthuyu baasi, ndi chikhalidwe chanu chonyongana inu a MCP. Ngozi ngozi ya chiyani apapa?