Email a copy of 'MCP says Malawi economy on life support despite inflation rate down to 8.3%' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP says Malawi economy on life support despite inflation rate down to 8.3%' to a friend
Aon Malawi, an insurance broker has finally rebranded to Minet Malawi following the acquisition of Aon Plc’s operations across several...
Mayi walankhula zogwira mtima…… Koma image iyi Ndiya Juliana Lunguzi
Economy iyenda bwino bwanji ngati anthu akumanga nyumba Ku Lilongwe Ku Maula ya Ndalama zankhaninkhani koma komwe atenga ndalamazo sikukudziwika. Economy iyenda bwino bwanji ngati anthu akutenga magalimoto a chipani nkupatsa ana awo, azipongozi awo pomwe anthu Omwe akuyendetsa chipani nkumayenda pansi.
Government, please do what has happened Ku Cambodia where the main opposition party has been outlawed because of their policy of revolt as Chakwera is preaching in Malawi.
Congratulations Mr Speaker Pokana kuvomereza zauchitsilu zomwe analankhula Chakwera mu parliament. Iyeyo ngati anataika m’manja mwa Mulungu asapangitse parliament yonse kutaika. Bravo Mr Speaker, keep it up!!!!
Business ndi Mulopwana ndinu Mbuzi za anthu mukanatenga zinthu zikuyenda mukutanthauzanji? Kapena Mai Anu ndi aja akumavina kusonkhano kuti azilandira ma K50 eti? Mbuzi za anthu komaso ndinu otembeleledwa ana a prince of thieves kkkkkk
Mulopwana is wombwambwana indeed. I wonder if you stay in Malawi. Stupid people like you should be ashamed of such sloppy thinking. I really wonder if your head has brain or is just a container full of shit
Low inflation is characterized with low or stable prices of commodities but why is it the that the prices are going up in Malawi with manufacturers citing high costs of production?????
Am not coming back soon
alephera a pitala
Ukuteta, Its only IMF and World Bank can ascertain your views but contrary to that, their reports says Malawi is doing well. Tisiye Nsanje amalawi. Ndizowona tikuwufunitsitsa mpandowo koma nthawi yathu sinakwane
Cement from mk6, 000 to mk12, 000.
Ndiye muziti inflation yatsika
Nanga anthu angadye Cement????
So kwaiwe zinthu zili bwino? You must be a dunderhead lomwe who thinks if he has eaten everybody else has
Just argue without mentioning my tribe please? Put your facts leave lhomwe out of this. U think alhomwe onse zawo Zili bwino Kapena ukuona ngati anthu osauka ndi mtundu wako okha? Or u think lhomwe are not worthy leaders?
There is nothing positive that will come from the Tambala Wakuda Party of darkness and killing. We who stay abroad appreciate the way the economy is managed and the inflation rate which has stabilized for long
Doing well what you fool? Do you stay in Malawi and see how stinking and suffering people have become?