Email a copy of 'MCP’s Chakwera cautioned over ‘power obsession’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP’s Chakwera cautioned over ‘power obsession’' to a friend
Muhammad Sulumba grabbed a goal for Nyasa Big Bullets in their 2-1 win against Red Lions on Sunday at Balaka...
The writer is an empty Tin.
Galu iwe udatumidwa ntchito yopusa
When has people welcoming their leader become” a power obssession ” problem? The people cautioning our beloved Reverend seem to miss a loint here. In any case Chakwera ks the keader of opposition and has the right to be welcomed by his supporters jjst like any leader in Malawi.
Security problem? Why only Chakwera? Nanga enawa akunenepa ndi misonkho yathuwa, samalandilidwa pa airport?
Chakwera deserve to be warmly welcomed.
muiuze mbuzi imalemba pa social mediayo kuti akuti ndiwe galu kwabasi
This is nonsense of an article. Mwasowa zolemba apa….. I can’t see any logic in your writing. Why can’t you feel pity with PM too…poti nayenso is obsessed with power. Our politicians share same disease and no one is better. So don’t be bias again.
You are still energetic.
Palibe nkhani pamenepa. Ndimayesa anthu amafuna kukachingamila mtsogoleri wawo. Ngati simutsogoleri wanu khalani chete!!! God’s time is the best because one day Right Honourable Chakwera will rule this country. DPP does not have the fate of Malawi but God alone. God is not man that he can lie. Wait and see how God will elevate O Chakwera.
Paja Chakwera Lazaro ndi uti ndipo amatani?
leave him alone, kodi kukumana ndimasapota kumabweretsa njala mdziko??
Kuponda manyi sikukula phazi, Kukula mphuno sikudziwa kumina. Kapena kuti Chulukechuluke ngwa njuchi umanena iyo ykuluma. Ndiye tisanamizanepo apa. Awina adzawoneka zisankho zikafikapo.