Email a copy of 'MCP’s Sitolo blasts DPP’s Ganda for refusing to take part in debate' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP’s Sitolo blasts DPP’s Ganda for refusing to take part in debate' to a friend
National Roads Authority Spokesperson Portia Kajanga has trashed assertions that the construction of the Thabwa – Chitseko – Seveni road...
kkkkkkkkkk. NYAMPHANJA wagwa kawiri kasala kamodzi. iwe u participate on the debate what is your manifesto. MP wa opposition sangatithandize ife. obwera ndi amene amapanga chitukuko for example olemera ambiri aku Phokera, Sorgin ndi Bangula ndi anthu obwera ndipo ndi amene akupanga zinthu zabwino than you called yourself mizika
Winning a Parliamentary seat for opposition bench will show the foolishness of the Sena people. Why wasting early hours time going to vote for an MP whom you know will occupy an opposition seat in Parliament?
Akuopa a DPP. iwe mwana wa kwathu sitolo wawina kale. ife nkwenya sitimuvotora. alendo tatopa nawo.
mwana wa kwathu iwe. mudzi wa brighton. ndiwe owina wina kale. awa akukuopa awa a Dpp. ife nkwenya iyayi. tikufuna mwana wa mmudzi.
Akudziwa kuti ndi oluza kale so no need for her to attend. MCP Boma!!!
Sitolo watenga kale constituancy imeneyo uyu kwawo ndi ku Mwanza
I am not surprised. It is their leader who tells them to snub such debates as he himself also snubs to answer questions in parliament. Mr. Ibu also recently snubbed the press conference on his way back from UNGA. Failed leadership so to say.
Sitolo has already made it to Parliament and he is confident to lead the constituency.