Email a copy of 'MEC announces Malawi Tripartite election date: May 21 2019' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

10 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mutharika
Mutharika
6 years ago

Kkkkkkkk mumati munati a nthiwatiwa inu kufuna kusintha date to September…Peter is a finished force. We are just waiting for the final punch and he is out

Tchopanomics
6 years ago

kaya ife ma tchopa tizavota basi

psyuta
psyuta
6 years ago

kkkkkkkkkkkkk !! Makape ena agulitse property for campaign tsopano.

santana
santana
6 years ago

Kodi inu a Ade nkhani yoti anakuberani mavoti mwayesa kozembera pochita manyazi ndikuluza? Wosangovomera bwanji kuti anthu anakukanani? Akuluakulu anu ndi ndani analongosolapo kuti mavoti ankabedwa njira yakutiyakuti. Ngakhale iweyo Ade sungathe kufotokoza m’mene mavoti anabedwera. Chabwino tangonena zavoti yako yokha kuti inabedwa bwanji. Kapena uphatikize ndi ya Kasakula kuti inabedwa chonchi. Tiyankheni tidziwe. Mukamachita comment bwalo lino muzitsitsa ma facts musamabere apa ndi half facts kapena kungotukwana basi. Tiuzeni mavoti ankabedwa bwanji. Komanso tiuzeni chifukwa chomwe a Malawi akhala akukana kuti MCP isalowe m’boma pazisankho zones zisanu ngakhale kuti inayimitsapo m’busa?

santana
santana
6 years ago

Mr Kaitano, mufuna kundiuza kuti 2014 m’mene munkati anakubelani kunalibeko zo Gjgula, Whatsapp, kapena internet? Koma mkulu munali mu Malawi mommuno? KOdi MCP pali chisankho chomwe siimanena kuti yaberedwa? Chisankho chilichonse nyimbo imakhala yomweyo basi. Kodi akamakuberani ma monitor anu amakhala alikuti? Kapena mumasankha ma monitor wosakhulupilika ndiye amakupangani chikuwawe? MCP chonde tipatseni zifukwa zokwanira zomwe mwakhala mukukanidwa ndi a Malawi mu zisankho zones zisanu. Munalakwa chiyani kuti a Malawi akuumireni mtima chotere? Anzanu anali kunja mwangozi kwazaka ziwiri zokha nkuwasankhanso kuti abwerere m’boma chikhalireni inu mumachita kugwada kuti akusankheni koma ng’oooo wosaohula kanthu. A Malawi adzakhala akukuwonetsani mbwadza chisankho… Read more »

Kaitano
Kaitano
6 years ago
Reply to  santana

Santana, you did not ask me that question, but to day i have the answer of your Question. Chiyambire cha multparty in this country, what people voted for was freedom be to all Malawians including you and your family. The reason why just to aline with your Question though it shows how young you are is that Malawi Congress Party is a Party that believes in Unity, 2014 very unfortunate that you don’t know even to day and i don’t think you will accept my answer that it was M.C.P who won 2014 Election, you can ask every one in… Read more »

Odala
Odala
6 years ago
Reply to  santana

Koma Santana ulintchito. daily komenting for dpp. sungapumeko and have different news?

Kaitano
Kaitano
6 years ago

At least, this is the way to go osati zija mumafuna mupange zija zomati September, mayi mukanaona mbwadza ndithu.
Tidazionela patali zimene zija, your wish was to side with your thieves to be given more days so that apange ma Ballot ena, hehehehe not these Malawians of to day.
Nthawi ya achina Santana kunalibeko internet, kunalibeko face book,kunalibeko WhatsApp, kunalibeko zo Gugula hahahahahahahaha!! lero paliponse, ndipo communication yaphweka iyi.
Ndiye ,mukamachita za fodya zanuzo dziwani kuti we are following you.

Ade
Ade
6 years ago

Let us vote this government out of power, I know now they are busy putting in mechanisms to rig elections koma this time sizitheka

Chilungamo
6 years ago
Reply to  Ade

Where will the supporters of the mighty DPP be when you think of voting this government out??? You must win their hearts fort and convince them to vote for your stupid lazaro. As it stands all you do is to swear and insult Peter and the DPP without giving alternative sound plans for this country. Mukumatikwananso a Lhomwe onse and you think you can win???. Mwauponda. If masapota a DiPhiPhi tizabwera mwa unyinji wathu kudzabvotera chipani chathu mwankokomo. Mulira simunati. DPP 2019 Bomaaaaaaaaaaaa!!!!!!!!!!

Read previous post:
Mulhako wa Alhomwe condemns newspaper column on ‘Tchopanomics’:  Mulli says stop ethnicisation of Malawi policies

The Mulhako wa Alhomwe cultural heritage has condemned the influential Backbencher newspaper column for a title of ‘Mutharika and Tchopanomics’, saying it...

Close