Email a copy of 'Merry Christmas to you all, but don’t do things as world coming to an end' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

3 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mkulu zikaoneka
Mkulu zikaoneka
5 years ago

@ Gwemula ngati ndinu abusa, mwaphonya msewu baba. Mukanangolalikira uthengawo osati mmene mwapangiramu. Anakuuzani ndani kuti zaka za munthu zikamachepa ndiye kuti basi akupita kumanda? Zoti anthu ena sadzaliona dzenje la manda kufikira mpulumutsi adzafike mukudziziwa?

Gwemula
Gwemula
5 years ago

Kodi vesi loti Yesu anabadwa pa 25 December lilipati mBaibulo mu komanso anthufe we are very blind zoona pa 1 January pano muzakhala mukusangalala kuti Happy new year!! Mukuiwala kuti zaka zanu zikunka zicheperachepera mmalo mozidandaulira kuti masiku anga akuthera kuchitseko inu basi busy happy!! Hahaha kuiwala kuti tikupita kumanda posachedwapa #Apa chenjezo langa abale tiyeni tilimbikire kupemphera kwa Chauta mwini moyo ndi nthaka ndi kumwamba kuti tsiku loima pa Maso pake akatinvere chisoni nkukatilowetsa ku Mparadiso #Mulungu potilenga anali ndicholinga #Kumugwadira iye basi#

Ras Shillo
Ras Shillo
5 years ago
Reply to  Gwemula

Iwe ulibe nzeru kwabasi kukula sikutathauza kupita kumanda. Anyone, anytime amapita basi. 25 december is just a symbolic date. Asiye osangalala asangalale osati maganizo ako akutuwo.

Read previous post:
Mutharika encourages citizens to remember where goodwill comes during Christmas

President Peter Mutharika has reflected on the important of Christian message of treating others with consideration and wish one another love,...

Close