Email a copy of 'MHRC investigating Malawi Police for shooting boy, 14' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

4 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
santana
santana
7 years ago

Ndakhalapo ku Boarding School ndipo ndimadziwa kuti beans and cabbage are often prepared. Kodi cabbage ameneyu anaphikidwa kachingati pa week imeneyi, nanga anaphikidwa motani? Chifukwa nkhani isakhale yoti chiwawa chinayambika chifukwa kunaphikidwa cabbage. Reporter, please elaborate. Do you mean anawo anangopatsidwa cabbage wopanda chodyera chake, nsima kapena mpunga? Sindikumvetsa pamenepa. Anzanga wowerenganu mukuimva bwanji nkhaniyi? Ngati ndi choncho Boarding master ameneyu afotokoze bwino.

youna
youna
7 years ago

Kodi a police athuwa alowa chiwanda chotani? Mmene akumenyera anthu ochokera kuzintchito mu Limbe!!!! Sakufusanso kuti kaya wapezeka bwanji pa depot, akungofikira kuthibula basi.

Dziko ndi Anthu
Dziko ndi Anthu
7 years ago

A James Kadadzera sibwino kukana pamene umboni uli pa mtetete .Apatu mwanayu mwamuphera ufulu wake okhala ndi moyo ndipo chilungao chichitikepo apa.
Mwana wa 14yrs ndiponso wa form 1 zoona mpaka kumutengera mufti?
Apolice mukutiyenjezatu mwamva! chomwe mungadziwe ndi chakuti simungathe kugwira ntchito popanda community.
Tibwenzeratu zimenezi. watch out mmawatenga malamulo kuwayika mmanja mwanu just because ndinu a Police, remember iyo ndi ntchitomunachita kufunsira and muthanso kuchosedwa komanso lamulo lomwero litha kukugwirani ntchito inuyo funsani anzanu.

nkhani
nkhani
7 years ago

Get well soon young man!

Read previous post:
Granny ‘witch’ gets mob justice: Malawi Police arrest five

An angry mob in Blantyre stoned to death a 73-year-old woman  for allegedly being a ‘witch’. The incident happened Tuesday and...

Close