Email a copy of 'Mia backs Kabwila for Salima North West, calls for MCP unity' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mia backs Kabwila for Salima North West, calls for MCP unity' to a friend
Malawi Under 23 national football team on Tuesday drew 1-1 against Botswana at the Kamuzu Stadium in Blantyre to progress...
Too TALKATIVE KABWIRA WHY?
Please Mr. MCP VP, go to Dedza and do the same for Juliana Lunguzi otherwise we will assume, wrongly perhaps, you are party to a diabolic plot by Chidzanja to remove her from the scene.
Well, it won’t work.
Then this should be the same with Lunguzi Juliana please Mr Mia
I like this woman (Jesse Kabwila.) in MCP, She is very strong. And we need more women to Parliament .
Kodi Bwana Mia simukudziwa kuti President Dr Chakwera sakufuna Kabwila? Mai ameneyi ndi nkholokolo. Akufunatu Phale kumeneko.
bBible limati konda mdani wako monga iwe mwini umadzikondera. Chotero Mia waonetsa nzeru za Umulungu ndithu. Komaso Jesse ndi Mzimayi chotero sibwino kulimbana nawo ayi MCP for 50:50 campaign
Bible ndi Mia zokhudzana pati?
Kabwira is a strong woman. I like her charachteristics
So, it’s now Mia, the new real leader of MCP, and not oChakwera calling the shots!
See? It has been said many times that oChakwera would be relieved of his responsibilities.
Fwetseke! Akati Vice President ndiye sakhala ndi ntchito? Mukuyesa kutizipani toyiyako democratic when there is no democracy at all. Kabwira had asked Mia to assist her, nothing wrong
Remember Kabwira was in Chikhwawa last month campaigning for Mia’s wife. Kabwira knows politics.
Inutu paja vp wanu Chilima anakuthawani chifukwa simumamupatsa ntchito
Inuso tamawerengani, Mia is the vice President of MCP, the word vice mwina ndi amene avuta kumveka eti? Ndili panotu kutsuka ubongo wanthu.
Its this mentality yomwe mumamukhalila nayo Chilima and no wonder he chose to go his own way! Is a vice president so useless on decision making such that he always needs to be told eveything! Nanunso inunso ndiye mpaka udzete wachonchi kuuwonetsela ku gulu? Paja sukulu mudalekela pati……………………..! Awanso nawoooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooo
Jessie for MCP and for Malawi – MCP for us all. Go Jessie!!!!!
Mia want Kabwira pamene Chakwera and MCP Supporters in the Constituency want Phale, hehehe ine yanga ndi UTM osati zamikanganozi
Nanga Ife zitigwedeze? Uli ndi ufulu wako, kapena siumadziwa?
Nanga mikangano ya ma primary oyamba in Mzuzu mulimba a UTM