Email a copy of 'Mia dispute MEC stringer’s report: ‘I did not endorse Kabwila's MCP parliamentary candidature’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mia dispute MEC stringer’s report: ‘I did not endorse Kabwila's MCP parliamentary candidature’' to a friend
Malawi Police CID Officers on Wednesday arrested four Tanzanian nationals on suspicion that they are connected to series of robbery...
Mumva naye kuwawa Mia…..apa Chakwera adasankha bwino osati Msowoya ongokhala phwiiiiiooi
MCP will never win an election. O Chakwera tiyeni kolalikira basi ufumu wadziko lapansi wavuta basi. I used to be MCP koma hmm
Zoooooona bwanawe mposavuta MCP kudzawina general elections koma kulephela kuwina election ya pa nyumba pa mtumbuka weniweni……………..kkkkkkkkkkkkkk Nanga zooooooooooooona pa anthu 17 million kamunthu kena kake basi kamvekele ndikulankhulila dziko lonseeeeeeeeeeeeee awanso nawo awa, paja mumakhala kuti kodi baba!!
Komatu Sidik Mia mukumva naye kuwawa, ndipo simunati mukhaula ndi umbava wanuwo muwona. Mmalo motifotokozela nkhani ya makina anapezeka ku Mozambique aja mufuna musokoneze ndi Mia? Mulibe manyazi eti? Palinkhani apa?
So its news because its Mia and was not when DPP endorsed all its serving MPs without primaries! MEC why the double standards? Pali nkhani apaaaaaaaaaa!! Kodi anthu mukuoneka Mia yu simukugona naye tulo etiiiiiiiiiiiiiiiiii
Mayhem in MCP continues !
Jessie akuoneka chonchi panopa? Stressed up!
Miya has the audacity to endorse his wife in mkombezi and his relation in Balaka , za ukaladi basi
Koma.kabwira popeza ndi munthu ndiye osayankhulapo mxiii
Ndipo tu mkuluyu anthu amudziwa mochedwa kuti aakuluwa nde eniake nepotism. he pushed his way to become MCP VP by corrupting Mr Chakwera, then he imposed his wife as a shadow MP in Chikwawa. as if that not enough he imposed another relative in Balaka west a shadow MP in the name of Harron Mia. Is this not nepotism? Akadzalowa m’boma all his sons, daughters and relatives adzawapezela tchito mu boma.
Kenako all his sons, daughters relatives adzawapezera tchito mu boma. After this he will go to his home in Pakistan kukatenga all his nieces and nephews. Maybe afterwards he may also call all his relatives from Afghanistan, Tajikistan, Turkmenistan, Kyrgyzstan etc etc onse adzadzadza kuno and be syphoning forex away from Malawi. Guys this is a time bomb, a disaster in the making, ine ndakuwuzani
Chimodzi mmene walizira alimi ang’ombe Ku lower shire kuwagula pamtengo wozizira abale ake achina Issa, Dassu.
A MIA TAWONANI ZIMENE MUKUCHITA, INU INU MUYISOKONEZA CONGRESS. MUSATENGELE ZERU ZA KU DPP NDI KUBWELESA KU MCP NDI ZIMENE MUPOYILISA ANTHU.
Mia is clearly not telling the truth here: he was quoted accurately; and as Kabwila’s supporters are concerned, this was to pay back Kabwila for her recent efforts campaigning for Mia’s wife in the Lower Shire. So, the denial by Mia simply won’t cut it.
Is it possible now that oChakwera is developing a spine to put Mia in his place, and that is why Mia came out to deny this?
Oooooh, leadership issues galore in the house of oChakwera!