Email a copy of 'Mia donates vehicle, breeding livestock to Malawi muslims' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
newest oldest most voted
Notify of
Zoona
Guest
Zoona

Ndimawakonda ayao kwambiri koma chipembedzo ichi mmmm pano chalowa chipolowe

pathfinder
Guest
pathfinder

Chiyao ndi chisilamu ndi zinthu ziwiri zosiyana madala. Chisilamu ndi chipembezo ndipo chiyao ndichiyankhulo, komanso a yao ndi chikhalidwe kapena kuti mtundu wa anthu ngati mmene aliri alhomwe kapena atumbuka. SI wonse ayao omwe ali asilamu komanso si wonse asilamu omwe ali ayao.Ndiye ngati umakonda ayao zakhala bwino. Choncho usawayipise ayao podana ndizochitika za chipembezo cha chisilamu kapena opembeza chisilamucho.