Email a copy of 'Mia says the future of Malawi is bright with MCP and Chakwera governing in 2019' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mia says the future of Malawi is bright with MCP and Chakwera governing in 2019' to a friend
Professor Patrick Lumumba of Kenya was once quoted as saying ‘a good dancer must know when to leave the stage’. ...
BODZA, BODZA, BODZA. Mia will be safe and guaranteed running mate position if Chakwera continues to head MCP and becomes Presoident
John Tologo zomwe ukunena sizikugwiriza D P P yamwetsa anthu manyi ku Lilongwe ndani angavotereso 2019 Dr Chakwera ndi Mia ndi Boma kale wina athawa
mukhaula a DPP mbamva zachabe chabe,
tamvutika mokwanila under pitala leadership,2019 tiwone zina
Nkaladi ndi nkaladi basi. Achipeta samudziwa. Uyu si hule wa dzipani uyu……kkkkk
Wina athawa chaka chake ndi chino.
Inu a Congress munya muobna. Mwakhaula nazo ngongole komanso kuba madzi a Lilongwe Water Board ndiye mukufuna mulowe m boma kuti mukabe ndi kumanga anthu nyakula kuti chipani canu chikhalenso ndi moyo, ng’ooooooo, sitikuvoterani. Chakwera please! go back to the church, Assemblies of God is missing you. Please forget about being elected as Malawi’s head of State. Akasankhe iwe ife tili kuti?????????
It is so nice to see Mia and Msowoya dancing together……..now I understand why DPP is spending sleepless nights with MCP……….
Muhlakho wa a Lomwe uli mmadzi ………..ndalama mukubazo come 2019 just make sure you have a better explanation otherwise it will be nyakula time you and your family………..this is MCP, you have been warned.
MCP woyee
Chakwela. Mia. Msowoya. We are on ur side