Email a copy of 'Mind games begin as Wanderers want to play Bullets at ‘home’ Balaka not Bingu Stadium' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
newest oldest most voted
Notify of
Mighty Be Forward Wanderers Fc
Guest
Mighty Be Forward Wanderers Fc

kalonga inkakakamira kukasewela pahome ndipo zinathekadi popeza kunali kusankhakwawo.ndiye wanderers nayo yapempha koma mwakana,zosadetsa nkhawa kwenikweni koma vuto ndi nkhani ya zachuma yomwe ili paliponse mu m`malawimuno ndiye tinziveranako zinazi.sikuti tikuopa bb popeza aja ndianaathu.ndipo tikwanitsa kukwapula mosawavelaso chisoni.come sartuday.

Peter Katasya Chintheche
Guest

Tiyenera kusewera pa home basi kuluza kuwina nde mpilawo

nyenyezi
Guest
nyenyezi

Nkhumba, mikodzo FC kuopa BB kumeneko ife anywhere you choose tikakupherani komweko mwamva m’mayesa munkati pa BNS ndi pa home panu nanga kero zatani kuti muzithawapo kkkk shame

Dodolido
Guest
Dodolido

At Bingu both teams will rake in mor money than they will spend for the game’s preps. So Nomads argument does not hold

Nox Nthambi
Guest
Nox Nthambi

It will be nice to play them in Balaka kuti akafere pakhomo kusiyana kuti maliro akanyamule kuchokera ku Lilongwe which will add more cost to the Neba hahahahahaha. NBB ndi moto……neba timadya ngati linunda

bamangwe
Guest
bamangwe

Mind games indeed, neba we know u r creating all these problems to deviate our focus kuti tidziti you are not preparing for this game. Look just last week u did the same complaining threatening that u would not go to play at karonga stadium but we were reliably informed u were already in karonga on Thursday to climatise. Ufuna upusise ndani, or utati game tikamenye mu mtengo tiri nawe kkkkkkkkkk

Mzozodo
Guest
Mzozodo

I don’t see any mind games here, mere proposing that the match takes place in Balaka to minimise costs? Ok, if you insist that the match takes place in Lilongwe, will you foot the teams costs from your pocket? I thought they are just trying to live within their means?

peter
Guest
peter

Mano home basi.