Email a copy of 'Ministers lose voice in political rallies to drum up support for govt in worsening economic situation' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ministers lose voice in political rallies to drum up support for govt in worsening economic situation' to a friend
Two girls are in Police custody at Lilongwe Police Station, for admitting that they were sent to Simama Hotel to...
Mothing national about loosing voicsz dus party rallies.
Bravo Henry Mussa for supporting DPP and APM.
Amzanu akuzindikira kuti anachita kutumidwa ndipo akalandira ka alawansi kawo akupita kumene kuli anthu awo. Inu muli busy kulondola masiketi ndi mbina. Mukazaluza muzizati atibera! Simukuseka lero, tiye nazoni ndi ndaletu izi. Amawina kapena kuluza. An early bird catches the worm. Hard work pays. Tili mbuyomo amusa. Osauka satopa. Thako limodzi silizipaka manyi. It takes two to pick a quarel. Akupakani koma inu zipukutani, ulendo ndiwautali uwu.
mmene zimakhalira ngati munthu ukamanama umabwebweta zambiri kuti mwina anthu okuva akukhulupirire kkkkk
This just shows that the ministers and MPs are not committed to their core responsibilities. How could they be going about conducting rallies when parliament is in session? And some stupid Malawians still go to attend such rallies and listen to the lies!!! huh! And mawu mpaka kutha chifukwa cholongolola kumamiza anthu. And you are not even ashamed of that asking the speaker to bear with you for your being irresponsible. Really!!! Only in Malawi
Nothing to say only god knows. bola kumwela zilibwino azanthu chakudya ndi mamkhwala mzipatala
Kunena zowona, dziko ili silizasinthika mpang’ono pomwe chifukwa anthu ake anazolowera kusauka. M’mene zinthu zinabvutira nthawi ya Bingu shuwa ndikusankhaso mbale wake prezidenti. Joisi Banda angodana naye. Anangolowa kuchokera kunja kwekweni zinthu ndikusintha m’masiku 100 okha. Anthu anayiwala zandale mpaka nthawi yamavoti itayandikira. Zosokonekera zachulukisa.
ha ha ha ha ha ha ha some one will collapse on the podium!!!
Munthu ulimanja tambalare mkumati boma likupatse chilichonse aaaa guyz tiyeni tiphunzire kuzidalira
And mavuto azachuma ndi apaziko lose or MCP itati ipasidwe mwawi olamuliranso mavutowa sangathe
Dpp is shit