Email a copy of 'Mixed views on splashing K300m for Malawi 51st Independence celebrations' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

60 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
kavwiza
kavwiza
8 years ago

Sasangalala kapena kukondwera pamene munthu wuli mumabvuto. A Malawi akubvutika kunjaku ma ambulance sakuyenda kamba ka mafuta pomwe in muli busy kukonzekera chitsangalaro what a fool

Wachikond
Wachikond
8 years ago

In my house we were counted 5 last census then it means give me my 100 thousand nkagule matumba 10 achimanga ndisunge zozakhala pa mzere kudikila 10kg ndiukapolo womwe kuphwandoko am not going

MAMA
MAMA
8 years ago

Pofunika a mcp ndi pp ndi wena nonse okufuna kwa bwino musazapitek

MULUNGU Ngwa bwino

Musa

box13 bilila NU
8 years ago

That’s too little ,vuto ndi kwacha ilibe mphavu imeneyo ma rand ndi 7.5million and u are lamenting, eeeee mavuto bwanji.

Novirikana
8 years ago

Masavage ambiri akuganiza kuti 300mita ndiyambiri. Akuyesa ndiyokonzekera ukwati osati national event. Koma abale sukulu ndiyofunika zedi.

Says the truth to shame Devil
Says the truth to shame Devil
8 years ago

Kasi apa mbwenu titenge vyalo vya kuwalo vitovwirenge nthena? Apa pakuyana waka ngati dada mulowevu uyo wakuwika kumwera phere ndalama panthazi kuluska kugulira wana chakulya pa nyumba. Kasi ka 300m tingagulako yayi ngoma kuti kuno ku mizi tisangeko chakulya? kweni wakuneneska kuti nyengo zinyake wanthu wanyake sukulu yikuwawowvira yayi. Nadi apa boma mbwenu lingaghanaghana yayi kuti malingana na masuzgo agho tili nagho tileke danga vya vikondwerero. Mbaya Mwe! Mama Malawi kulongozgeka na wanthu wambula mitu.

Namaloko
8 years ago

Lets divide K300,000,000 by 15,000,000 people. Each person will get K20. What are
we going to buy with the K20? May be jiggs. Let us use the money for celebrations becoz every Malawian will be invited to attend and watch free football match that does not worth K20. Billy Mayaya can you petition the govt. to increase the allocation. K20 is just too low.

Jokujoku
Jokujoku
8 years ago
Reply to  Namaloko

Then devide 300 000 000 by 8000 000 it will be 37 .5 which can build 37+ school blocks..what about that

Chimani. Game
Chimani. Game
8 years ago

Remember Joyce Banda.this idiot of a president called peter doesn’t know what he is doing.very greedy and proud

zibwente
zibwente
8 years ago

300 million is not enough for national celebrations. Zimafunika kuzipepesako nthawi ina. Kodi bwanji a Malawi kudandaula. Ndalama izi ndichimozimozi ndizomwe Beckham anaononga pa birthday pa mwana wake pamene if its the nation of 15 million people.

mavuto
mavuto
8 years ago

Please use the money to buy maize for the hungry people who were affected by the heavy rains. People will love you and respect you for that.

Read previous post:
Insurance Institute LL Chapter declares games a success

The Insurance Institute of Malawi (IIM) Lilongwe Chapter has declared this year’s Sports Bonanza a success, hailing insurance companies, brokers...

Close