Email a copy of 'More at risk of preventable deaths: Malawi hospitals facing services scale-down' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'More at risk of preventable deaths: Malawi hospitals facing services scale-down' to a friend
The Ministry of Gender, Children, Disability and Social Welfare is mobilizing women in Civil Service Commission to form professional networks...
Kodi a Kapito alipo Ku Malawi?
Which DHO can call a nurse like you. A shadow minister amenewo. Badikirani…………Sonkherananitu ma allowance aja mwadya 9 weeks. That’s what happens with Cash Budget. The whole shadow minister does not know this………………….Shame………Just tell the Malawi nation the truth not politicking
tikhonza kuyankhula izi ndi izo koma tonse tikutha psyiti. Sizinafike pakolasi,zipani zilamulira zambiri palibe chitazasinthe,watch out yesu akubwela posachedwa.
Tidapita pa chipatala chodziwika cha m’boma la Zomba.Adalemba bwino lomwe mankwala amphumu(sulbutamol), adatipatsa bactrim ndi asprin. Titawafunsa akuluakulu,adangotenga mankwala oyenera nkutipatsa.Akumidzife tili pavuto lalikulu, TIKUFA!
Pitala ndi alomwe anzake asiye kuba and the rest will follow suit in Malawi.Ngati kuba kumayamba ndi anthu akuluakulu with all the benefits under their feet,what do you expect from an ordinary struggling worker?Its has become a norm in the civil service to steal to make ends meet.
Peter mwalephera boma tangochokaniponi pampandopo
The Health sector in Malawi is crap.Very few doctors to carter for the bulging population.Some crooked pharmacists sell drugs to private hospitals.No proper funding to hospitals since everybody in higher positions is concerned with self enrichment.Poor diet for patients.Hospitals are killing grounds in Malawi.Nothing is working in this impoverished country.Lunguzi pump some senses into these dunderheads.They don’t seem to have any idea on health sector.They are politicising everything.
But closely monitor the so called health worker not to be stealing drugs yet the hospitals are struggling.
Kunonso ku Karonga a chipatala afika pena pake poti ay, zosayenda. Kukhalira kupemphesa koma ili ofesi ya boma. A Malawi, kuba tisiye. A ndale musiyenso dyera kuti ndarama zizipezeka. Anthu opeza bwino azilipiranso.
Iwe N0:21 ngati umadya nowo mamphemvupevu khala chete ndizokhudza amphawife izi osoti agulukunyinda ngati inu ndi mbava zopanda chisoni zinzakozo.