Email a copy of 'More Malawians return from S. Africa: Mutharika opts for diplmatic talks with Zuma' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'More Malawians return from S. Africa: Mutharika opts for diplmatic talks with Zuma' to a friend
Mighty Be Forward Wanderers have finally completed the signing of impressive Cameroonian striker Lionel Assu after paying K1.4 million. His...
Everything will be solved and you will be back.
Evrything Is Posble With God,lets Ask God 4 Our Faila And What 2do Zatsopano.
Ikawele chenene boma jikajigale mabus gethu. namboso tukumbuchile kuti anduna awechete yantengo S A bus was chipa whynot ah bola aiche kumusi
Don’t worry tikulembani ntchito
Mulungu akusungani bola moyo.
Ndukusapota bola lathu la malawi paganizo labwino lotumiza ma bus luno ku RSA kuzatenga anthu awo chonde zimenezi musazasiye
Kwacha yakumala nd yovuta kuyipeza nde tzitan tbwereranso tzikadya chicken
Tivomeleze kwathu ndi kwathu. Anthu mukagwire ntchito popanda ma documents aeni ake angakondwe? Timaona ku kia ma depotee every week which shows anthu alibe zowaloleza zokhalira mdzikomo. Akangotsika wk inayo wautali. Zinazi kumazion guys. Ndiye wina aziti tisagule ma shop awanthu a ku SRA zooona? Iye dzana mnamuona momo. poti ali ndi posungira kutipusitsa ife amu sigerege kunamichimba kwa mgona kwacenti ku mtandire komaaa umphawiu ndiumbuli mxiiii zonyasa. kukhala ngati ku sa anthu ama shop ndiwo akupanga chipongwe. mmayesa ndiamene amalemba ntchito ma foreigners ndiye mukuwanyozaso ngati zikuwakhudza. zinazi ziganizani. anthu akuchita chipongwe ndi anthu oti alibe chirichose akuba. sizothetsa… Read more »
My fellow Malawians, no one I say,no one is or will be happy in a foreign country. Malawians go South Africa it is because of poverty and high unemployment in Malawi. For 51 years since independence Malawi is still poorest in the world because we didn’t have leaders who were patriotic. Our leaders don’t love us at all but themselves and their families. Malawi needs a leader who loves the people and the country. That is why I sometimes say that our country is cursed.
Kuno kujon tili kunkhondo yolimbana ndi umphawi tikanalipo,kumalawi kulibe ntchito asaaa oremera akungolembana ntchito pachibale tikupanga ma rand ifee