Email a copy of 'Mother dumps baby in toilet for fear of SA-based hubby' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mother dumps baby in toilet for fear of SA-based hubby' to a friend
A man in his 50s only identified as Magombo was dumped dead about 100 meters from his house without a...
Mijomba its Mijomba basi will never change posinjana
Don’t give back the child to her inu a Social Welfare. Place the child ku institution as you are identifying a foster family for the baby. The baby must be fostered and then later adopted. Never give the child back to the mother even bele lake asayamweko angampasire matenda poti mwanayo sanachilire kuchipatala nde sitikudziwa status ya mayi. Munthu wachabechabe uyu.
Iwe ukuziti mtumbuka, mijombayo kuchindanako zolakwika, poti mahule ambiri tikuchinda mulilongwemu ndi atumbuka simumachinda mokwana mpaka akumathamangira mijombafe ndiye tikuwachitadi kanthu. ambiri akumakhala ndi zokoka hahahhahah
inu mumangopanga mapuleni anu , simumadziwa kuti mubelekapo pamenepo ? kumva kutsekemera kumeneko?
Ntchito za mijomba izi. kukonda kuchindana
Other Recent “Misunderstandings of Islam” 2016.05.01 (Turkey) An ISIS suicide car bombers detonates at a police station, killing two officers. 2016.05.01 (Iraq) Several children are among over three dozen dead when two suicide car bomb blasts go off in different areas. 2016.04.30 (Iraq) A Sunni suicide bomber sends two dozen Shiite pilgrims straight to Allah. 2016.04.29 (Syria) At least fifteen worshippers are killed when Sunnis shell a rival mosque during Friday prayers. 2016.04.26 (Philippines) The severed head of a Canadian retiree is found seven months after his capture by Abu Sayyaf. 2016.04.25 (Iraq) A family of seven, including two women… Read more »
Mwanayo ngati alipo andipase ine ndimulere ukananena kale panalibe bvuto
O…………………………………………………………………………………………………………………………………………………………….O
Iweyo ndi ndani?
If you mean your word, why not a mobile number or an email address so you can be contacted? If you dont mean your word, why say it?
Nanga, what good does it do a man to show him/herself up but hide in plain sight?
O……………………………………………………………………………………………………………………………………………………………O
Government should come up with a law kwa amatchonawa makamaka omwe amasiya akazi awo.Becoz kuno ku Malawi,pafupifupi akazi onse amakwatiwa n’cholinga chokabereka ana basi kutchona kusapangitse wina kukhala kapolo pazofuna zake.Mind you nature is very difficult to control.Apolice chonde muwonetsetse kuti Mercy asamuchite mwana chipongwe china.
Mothers are supposed to love their babies, where is the LOVE?
Komanso ma condom bwanji or Depo? Kupusa!!!!
Anakali mfana munthuyu. Anakwatiwa+kubereka ali mfana magazi athamanga heavy. 4 years opanda dalazi ndi mbola. Maganizo a Chifananso dii. Mnzimu wa munthu ndi oopsa.