Email a copy of 'Mozambique kicks out Malawi Police, tax body MRA out of territory ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mozambique kicks out Malawi Police, tax body MRA out of territory ' to a friend
The Ministry of Health says it is prepared to contain any diarrhoea infection caused by water and food contamination, following...
Shaa! Koma tilibedi mtsogoleri ndithu. A Malawi tasanduka a laughing stock. Malawi is now a standing joke of a nation.
If you had agreed to move by 31st December why stay put waiting for an eviction. Thats so embarrassing.
Guys, Peter akutichotsera ulemu dziko lathu. Sadly this is not a problem for him, he is too old and ancient. It is us and the future generations whose diginity is at stake.
Vuto a Malawi kukonda kuba, inu simungamage malo anu kumalawi konkuno abwino ndalama zonse mmantolera mmabodamu . achitabwino kwambiri bravo mozambique govt, aphuzilepo agaluwa kuti chitukuko sikuba,
KOMA AMALAWI KUPEPRRA CHIRICHONSE CHIMANGOTIVUTA, KODI BWANJI OSAMA CHANGAMUKA BWANJI, ETI AZITIPOTSA ANTHU AKU LIBERIA,SIERA LEONI OMWE SIKUNALI KWAO ANKANGOTAYIDWAKO AAAA
Kulanda zochepa zomwe Malawi alinazo