Email a copy of 'MP Gaffar under fire from constituents: ‘I will join DPP to win back the seat’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

14 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Wokhaula
6 years ago

I’ve tilinayo MP was DPP palibe chitukuko onse maphungu athu amadalira CDF ndi LDF ngati boma silinaike ndalama zambiri Ku counsels palibe chomwe chingabwere mudera lanu ngakhale uli Ku boma

Shasha
Shasha
6 years ago

Iyeyo Issa yo si ngero ayi koma akuyesetsa pa size yache, koma bvuto la independent ndaona kuti guidance imachepa coz ndi chipani ma program amakhalapo ambiri from nec, region, districti nde kupita Ku DPP is good decision chifukwa akhala ndi full party structure yomwe azimuuza zochita pa ground, koma mcp kugulitsa kwa mcp ndikobvuta ndi history yawo kunoku Ku mwera tinaona zokhoma mu ulamuliro wawo nde congrats lowani osachita mantha a mp, onena anena zitha, koma DPP nde dilu

Uziona
Uziona
6 years ago

Lowa DPP yo… Uziona. Kumaiwelengatu!!!!!!

mbobo
mbobo
6 years ago

Maonedwe anga in Malawi tiribe Mp wa 100% ayi, chimkana ma President same same, Ali ndizofooka zawo zambiri, ine ndi wa Dpp 100% APM koma Issa sanatukwanepo munthu olo during ma campaign amamutukwana ndi opikitsana naye nde saying his rude kaya, nde Issayo is not 100% koma ndiwozichepetsa nyamatyu timakhala naye maliro, zikwati, mipira, amayesetsa kuyendera mdera not daily angakwanitse ndani full time mu constituency is no joke, daily Ku nyumba kwache ndimamuvera chisoni anthu, bwana fees, njala, matenda, maliro transport, ma box, simply his humbo man, u know ondandaulanso sangalephere coz zina sakukwanitsa coz Ife anthufe too much kufuna… Read more »

mbuyache
mbuyache
6 years ago

Ndaiwala mijigo a Water for People akukumba mijigo mu constituency ya Issa Pano mdera la TA Ndakwera, anali kwa TA Maseyanso Pano akupitanso kwa Paramount Chief Lundu, nde madzi nde in next six months madzi akhala mbwe mbwe, a Gift of Givers anali momonso kukumba, kwa Nyamphota, Sekeni ndi Dyelatu apindula ndi new water budget akufuna aikhe ma water kiosks menemo, nde wina wati he wants to use Dpp, asaa mzeru ulibedi zoona, keep it up, Dpp yomweyo kuti wawawa

mbuyache
mbuyache
6 years ago

Issa mukumunenayo tiri naye full time mu constituency mu nde Si onse angamukonde nde democracy ndi imeneyi, komanso kumati sanaoneke, if he fails to go Ku Palament mumunenaso nde nothing chabwino, ndi waulemu wache nde chipongwe munenachi anachitira iwe wekhatu mwina, wagulidwa kuti umuyipitse, pepa, kwaonso nkochita bwino nde mwati Ali ndi financier, hede hulu, ayi dziko ndi imeneyi a Mp pitirizani kusatithawaku, adandaulayo mwina munamumana ya green, ddf mwamanga ma block 3, illovo 1, ma under 5 mbwee, Mukumanga cdss Ku Ndirande, magetsi akuyaka kwa Tomali ndi Ndakwera, Pano mumatiuza kuti Boma lavomerezanso magetsi Ku Ndirande ndi Mandrade, full… Read more »

mbuyache
mbuyache
6 years ago

He is full time in his constituency and being independent is not easy its a good move to join Dpp and also no one is 100% but he is trying his best but I feel author is an mcp sympathiser that’s why and they thought his going there, if he fails to go to Parliament u will brush him too, so palibe chabwino, not all will be happy with his move but we are, I feel the heading has been sponsored by pipo who despise my mp, sanati amunyoza but that will just make him stronger n wiser, Dpp Woyeeeee

Guantanamo Bay
Guantanamo Bay
6 years ago

Each district must benefit directly from revenue govt collects from that district. Its immoral to hv money collected from CK develop LL while the CK population remain poor. This proposition is what we call “federalism”. Tea from TO and MJ has develop BT. Tobacco from KU and MZ has developed LL. Uranium from KA built Ndata farm.

CHAPWE
CHAPWE
6 years ago

BASED ON THE ILLOVO COMMENT, IT SIMPLY MEANS CHIKWAWA PEOPLE NEED FEDERALISM SO THEY CAN UTILISE RESOURCES FROM THEIR AREA FOR DEVELOPMENT!!

Hlabezulu Ngonoonda
Hlabezulu Ngonoonda
6 years ago
Reply to  CHAPWE

Chapwe, not necessarily that rather that sugar, which is exported outside Malawi, started contributing to export earnings increase of 65% in 1966 thereby generating a positive Balance of Payments (BOP) in 1967 and remained so for the next five years. It resulted into the total value of exports exceeding the total value of imports. Much as it accepted that Chikwawa has not benefited from ILLOVO directly, it is proper to say that revenues being generated from sugar do find their way into development projects in the districts through Constituency Development Fund; Local Development Fund; and District Development Fund after being… Read more »

Murupale pa Thyolo
Murupale pa Thyolo
6 years ago

Mp ntchito yake si yachitukuko. That part is for Councillors. The people just want to milk him full stop.

jen
jen
6 years ago

Can you say that again bro. Millions of Malawians are ignorant about this truth.

Read previous post:
Malawi Minister says deported dubious Indian investor would not be allowed to come back

Minister of Home Affairs and Internal Security Grace Chiumia has said  a dubious  Indian investor who was deported  will not be allowed to...

Close