Email a copy of 'MP Malola challenges Mia for Nkombezi Constituency' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

10 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Jacobo John
Jacobo John
5 years ago

LL imamupweteka a Malola nde bvutodi lalikuli otherwise ndi ochezeka komanso o Dekha kwambiri nde pull up your socks khalani ku mudzi nanga ntchito Ina mulinayo kuposera apa ngati, Sidikiyo ndimunthunso atha kuluza koma ziri ndi mene mungachitire cos Sidik amangodalira cash basi, Sidik nseu wopita ku Makande kwao zaka zonsezi kulephera kuikitsa tala ndithu koma anali ku Unduna womweo eeeeeh

Charlie Thenesi
Charlie Thenesi
5 years ago

Bvuto la Malola ndiloti kwa Ngabu kaya amadana nako kaya his never they bwenzi atamukonda kwambiri more than Mia koma always ku LL amango siya mkazi basi nde iripo battle moti atha kuluza ngati angaime Sidik koma ngati iri Abidah mkazi wache kapena wina ku mcp eeeeeh Malola atenganso

mbuyache
mbuyache
5 years ago

Hon Malola ndithu ayesesa olo asali nduna, kuthandiza ana amasiye, bridge pa Lunkhwe, Technical college pa Ngabu anyamata aphunzire ma luso, ma brigde pa Nyakamba river just to mention pang’ono

Napoleon muza
5 years ago

Papa nyumbo Ida akuti chani? “ LOZANI ZANU KUTI TIONE” indeed let Mia point out what development he did during his tenure of office. Ntchito zake munthuyu zikumuikira umboni.

Viva MCP
Viva MCP
5 years ago

Kasaila alipo??? zukhala ngati walowa UTM. Mia simumutha.. .

kaka ni dada
kaka ni dada
5 years ago

Mukumuwopatu Mia, mwasonyeza nokha apa, msonkhano onse kukhalira kunena za Mia. Mutu sukugwira eti!

Duli
Duli
5 years ago

Up with Hon Makoka. Nkaladi must fall. No interest in the issues of anthu akuda.

Joovido
Joovido
5 years ago

Development comes through government who are funded through our tax so what do you want to tell us

#DzukaniAmalawi
#DzukaniAmalawi
5 years ago

This is the best way to fight the fight. Listing past successes is always the best way to demonstrate capability to take Malawians forward.

Namwera
Namwera
5 years ago

Kasaila is a sober and brilliant guy but you certainly don’t belong there where you are. You belong to the UTM

Read previous post:
Bwalo Likule promotion excites TNM customers

Customers have expressed satisfaction with the ongoing “Bwalo Likule” promotion aimed to reward customers for supporting its growth ambitions of...

Close