Email a copy of 'Mpinganjira flops at Wanderers polls: Top brass unopposed in free, credible elections' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mpinganjira flops at Wanderers polls: Top brass unopposed in free, credible elections' to a friend
People’s Party (PP) third vice president Kamlepo Kalua has told former vice president Khumbo Kachali to “stop whingeing” about the...
Sulumbaso mkachani olo atapanda kUchoka Bullets simians
komanso kumapemphera makosana mpirawonso usatiiwalitse .
‘returned??’
Nyerere woyeeee… Chitimu ichi, Aliponso wins. Free, fair and credible voting, ndindani angapose nyerere. Umodziumodzi 2016 TNM tikutenga komanso baclats….kkkkkZikuwawa iwe wosatifunira zabwino. Malunga that’s team soul, timakunyadira ngakhale wapuma. Umawanvetsa kuyabwa anthu enawa. Osafooka maplayer athu. Tisapota mpaka kholingo lichokemo. Nyerereeeeee……for life.
Chipi Mpinganjira is power hungry!
Ku mpira kuluza! Ku chipani kuluza!
Osangodzitaya bwanji?
Gaffar wonetsa ukulu wako anyasa asatenge sulumba,
ok.bola tione kusintha
Guys,Nyerere ndi michonya 4eva-!!!
Mafuno Abwino Kuti This Year Titenge TNM
Kodi Sulumba mudakamufuna eti Kkkkkkkkkkkkk I thought mumayelekedwa kuti anatha. Munya chakachino. Nyasa BB more fire neba anya season ino