Ndi zimenezo, dzinalo Mpinganjira says it all, njirayo aiwonadi ya zipani.
George Madondo
8 years ago
Mpinganjira kikikikiki the name says it all.Njirayo ndiye aiwonadi.From this party to that party.
PUTEN
8 years ago
Banja lomwe limayamba angongole alipakhonde limathatso angongole alipakhonde
monsieurstevefundi
8 years ago
Malawians are tired of politicians who are like kites, they go where the wind is blowing to. Sosten, BJ, Harry, Khumbo you are all traitors.
Dennis Manjolo
8 years ago
Chipani cha PP chatha ngati makatani. Nanga msogoleri wake kungopita kunja mpaka pano osabwera. These pipo are making nice decisions. ATHA kumakaweta ng’ombe za mkaka and will make a lot of money.
Nyamata wakwa Mayaka
8 years ago
Mr Mpinganjira mukafike bwino. Ifenso uvice president timaufuna.musambekezere kuti mudzawinanso mdziko lino ai
All those who r leaving PP are confused pipo. We all kno who is Mpinganjira. Amwene awa siofunika kuti Amalawi tiziwakhulupilira zonena zawo and am not sure if he’s a true born again. Amai osadandaula coz zimene zikuchitikazi mulungu akukukonzelani anthu oti mudzapange nawo campaign ya 2019 mwa smart.
CHISHENEMESI
8 years ago
Nanunso A Mpinganjira Simumaganiza Simudziwa Kuti Ndale Za Ku Malawi Kumathamangira Kumene Atenga Boma Nthawi Yomwe Ija Analuza Mai Aja Mukanaitulu Kupita Ku Boma Osafooka Dilu Ndi Amene Watenga Boma
Gwede
8 years ago
Apart from the perception that Mpinganjira is a ” Tidye nawo” There is something terribly wrong with the leadership style of this woman Joyce Banda ! The nearer people get close to her the more they discover it not all the Vice party presidents who have been forced out or resigned for unconvincing reasons can all be wrong ! The list includes Mr Cassim Chilumpha ( the only one popularly elected at a Party Convention ) Mr Mia (elected at a convention with her blessing ) Mr Khumbo Kachali (elected with her equivocal support) Mr Harry Mkandawire (appointed) Mr B… Read more »
Sake Chilling
8 years ago
What is the origin of the tag “Firebrand” for B Mpinganjira?