Email a copy of 'MPs in UTM relocate in Parliament. Shanil, Kaliati, Nyalonje get new seats' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MPs in UTM relocate in Parliament. Shanil, Kaliati, Nyalonje get new seats' to a friend
Malawi national team coach Ronny van Geneugden’s (RVG) has played down a sustained push for his resignation, saying he is satisfied...
OSADANDA
Mukumva nawo pheni?
What about Lucius Banda, Allan Ngumuya ali mbali iti? Abwelera pambuyo eti, chiifukwa saakumvekansotu matukutuku.
Iwe zipanga zako ndi maliseche akowo usalimbane ndi ife. Savage cadet
kkkkkkkkk iiiii aise ukandinena savage chifukwa sindibabayika ndi zinthu zazing’ono ngati UTM? hahahahaha Mwayamba kupsya mitima ngati mtsogoleri wanu Chilima eti? Munya muona ife a DPP timamenya ndale zenizeni osati za ana osapola pamchombo ngati inu, kapena thewera likutsina kkkkk koma ndiye ndaseka.
Ayi basi mukhululukireni Bwana, azipanga zache ndi chani chake?????? Kkkkkkkkkkkkk zovuta ya Boma liri njenjenje with the new kid on the block.
As the saying Goes, Njobvu ikamadutsa m’mudzi agalu amangokuwa, takunyadilani
A point of correction Mr editor/author; this country has never ever been ruled by Mr Dzimbiri, then mention a maid name of this Patricia
Muwava kuwa ndithu, mwatisangalasa kwabasi koma sagona tulo
How many Members of Parliament has the new party UTM?
Komaliza to be in parliament. Mwakwera bus zakutha za UTM.
Why are you bothered? It is their decision.
You are the one who is bothered. Who said it’s not their decision?
you can’t notice it in the language? why should some be concerned about the bus imene anthu akwele. You are one of the millions Malawians who do not think.