Email a copy of 'Mr. President, more kisses please! Malawi First Couple' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mr. President, more kisses please! Malawi First Couple' to a friend
Leader and founder of the Enlightened Christian Gathering prophet Shepherd Bushiri has been named president of African Christian Coalition for...
Vuto apa palibe. Anakisa azikazi anu. Ndinthawi yake
pali nkhani apa? anthu asa kisane…. vuto ndi chani? kisanani poyera ma hope a freeze kumene……inu koma zogololo ndi akazi aeni mxiiiiii
kiss imakolezera chikondi inde koma kiss yamalovu pagulu siyabwino or pangono bola yapa tsaya osati mpaka lilime mkamwa aaaà president?? its private love.
Yes very nice
They are not commiting sin. They are lawfully married and there is nothing obscene. Whats wrong with people? Some of u who are against this love act ndi ma jelasi basi. You have never kissed ur wives koma mahule. Leave APM andhis lawgully wedded wife alone.
Mr. President ndiye kufewa kumeneko
Me like
Kaya bolani ali pa banja…. Za kiss zo ine ndie log out…kkk
Anthu odya maliro sayamikira aliyense ngakhale atachita bwino bwanji.APM ngakhale akasanduka mngelo mkumakwera kumwamba ngati ELIYA wa mBaibulo Anthu bwezi akuti walakwa President sapita Kumwamba .Anthu ozolowera kudya matewera wobibirawa sitingawadabwe.
Nkhani yake ndiye iti pamenepa mwasowa zolemba eti president analakwa chiyani mkaziyo ndi wake ambilinu mudachitira umboni ukwati wao ndiye pa valentine asapatse kiss kwa okondedwa wao walakwa president pagulu pagulu ndiye kuti chiyani.Asanakwatile ndinu nomwe mudampatsa maina ambili mbili lero ali ndi mkazi bwanji akupeleka kiss pa gulu a malawi sitidzathekanso ndife dzitsilu dza wanthu mbuzi za mano kusi godemeti