Email a copy of 'Msaka in Eastern Region blazing whistle stop, urges people to register to vote for DPP' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Msaka in Eastern Region blazing whistle stop, urges people to register to vote for DPP' to a friend
Innuendoes are awash on social media in Malawi, suggesting that the governing Democratic Progressive Party (DPP) vice president for southern...
Imeneyo ndiye DPP osati zinazi munthu yekha yekha kupangisa misonkhano ma whistle stop ,koma ziko lonseli mulikwanitsa? tikuwonerani ulendo wa ku opposition basiii .Zikomo kwambiri poyambisa timamovement topanda pake ,mwawagawa mavoti a chakwera Apm tikuzawuka nthawi yomweyo
We dont see the people who attended the meetings so that we appreciate the ecstasy…..all we see on the photos above are DPP officials. Otherwise this is sensational reporting
Sangakuwoneseni akuwopa mukomoka 2019 isanafike hahahahaha. Kunali munthu kapena kuti chinamtindi chawanthu.
DPP lero so zazii it’s out of fashion UTM boma basi
zazii munthuso lero DPP out of fashion UTM boma basi
Udf will be wiped out kutha ngati nsalu ya makatani from 93 seats to two. Bakili is responsible for most of the bad things we are facing including theft of our taxes, poor roads, poor education standards, poor infrastructure, ndale zotukwana, political violence etc.
Ndipo tikalembetsa kumene bwana… inu osadanda… tikukudikilani kuno ku Mangochi
Bwana VP ER izi zikuyenda. Uthenga wanu taumva bwino and anthu akutsatilani. Simunyoza munthu mumangokamba mfundo. Bravo.
waste of a vote for these thugs!! better to try something new
ZOn a koma so zonama kkkkk