Email a copy of 'Muluzi presents Green Media Awards to Malawi environmental journalists' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Muluzi presents Green Media Awards to Malawi environmental journalists' to a friend
Malawi's Minister of Gender, Children, Social Welfare and Disabilities, Patricia Kalaiti, MP, on Thursday held three separate engagements with NGOs...
Mayo mayo ine !!!!! (crying) chilengedwe chikutha pamene ena akudyere momwemooo mayoooooooo!!!!!!!
A waste of resources. What have they reported worth getting awards?????
Anthu amenewa amalemba ziani pamene chilengedwe chiri kutha! Zoona Rasta (No.1). Nkhalango, ndi nyama zamthengo zikutha atola nkhani osalembapo kanthu ai. Lero akulandira zikho za chani-amene agula zikho izi angofuna kuchuka basi pamene chilengedwe chikutha-za show biz basi.
While the gesture of awarding Environmental Journalists is a welcome idea, but Malawi needs to do more than just this in order to save this beautiful country. Malawi was beautifully Green during the process of developing the National Environment Action Plan (NEAP) in the early 90s. But now it is almost a desert. It is easily visible as you travel from Lilongwe to Blantyre. As a seasoned Environmentalist, I feel ashamed that we have failed the Malawian people.
Mukulimbikitsa kulemba nkhani mmalo molimbikitsa chitetezo cha nkhalango ndi a Polisi. ma gaurd a forestry nawo ndi ma WOOD GATE.; Palibe akuchitapo choteteza. Chinanso a boma mukukweza kwambiri magetsi mumati anthu aziphikira chiani. anthu akulephera ngakhale kuitanitsa magetsi chifukwa cha kukwera mtengo. Anthunso tanyanya kumangodula mitengo chisawawa ngati Mulungu namalenga sanakuuzeni kuti musamale chilengedwe. A boma mupite pa zalewa road block a police ndi aforestry akungogwira amene alephera kuwadisha. Chikhalilecho pantunda paja anthu akugulitsa akuwona osalanda. A muluzi chitani kanthu.
Comment number 2 by this Dr. seems misplaced. Not so?
Let me start by thanking Nyasatimes for exposing this issue despite the fact that it is involving a high ranking official.
What baffles me is that Mcheka Chilenje is a very humble lady so I don’t understand why Mr Nkhoma wants to marry another wife.
But Kita was right to stop the issuance of the certificate becoz that was indeed against rules of natural justice.
God should forgive us indeed.
What?????
Nkalango zikutha inu ndi kumalandila ma award achiyani. Kabwenzeni poti palibe chomwe mukuchita. Inunso ndi amene lkumagula makala heavy, koma nkhuni mwa Senzani. Ine nditakuzalitsani kaye mitengo kaye osati zachibwanazo.