Welcome zain
wahidu llah, fimaliyakinah.
Allah akbar
titani
9 years ago
I, Brave Sinjani, knows him personally and warmly welcom him there at home and has to free; The warm Heart of Africa
sabiti
9 years ago
Amene zamunyansa akakolope nyanja Zain adzaimba basi kaya kunyoza kaya kusanyoza koma zichitika basi ndipo asilamu tiri pa Mw pano mpaka mudzatisiya mmene anatisiyira agogo anu
tuvitwana
9 years ago
Am Catholic but I enjoy his muzik. He’s good.
jonh
9 years ago
AMALAWI KODI BWANJI MUMADANA NDI IMFE ASILAMU MUMAFUNACHANI KWA IMFE BWANJI OSADANA NDI MA SATANIC AMENE AKULIMBIKITSA NDI KUKOLEDZERA ZIWAWA PA DZIKO LAPANSI MUZIKHALABE CHONCHO ,CHIPULUMUTSO MUKUCHIWONA KUTI NDI ICHO ZANUIZO MUSIYENI NSILAMU NZATHU AZATISANGALASE IMFE MUDZINA LA ALLAH ZONSE NDIZOTHEKA.

I lyk hs songs
I.a lets make duaa his coming leads to hidayah for all of us
Asatipusitse akufuna kudzameza bomba ameneyo
sono asilamu akumalawi inu muzatha kuvina house kapena kwaito ya joni? inu simunazolowera sikili
Ngati sukudziwa kalikonse ndibwino kukhala chete sunapuse sukhala ochenjera chifukwa choti wa komenta ai kupusa kwenikweni chifukwa ndiwe mbuli pazinthuzo, ochenjera amangochita research kuti azindikile za chipembedzocho osati kunyoza mwachidule malemba amati usaweluze kuopa kuti ungaweluzidwe komanso kodi ndindani mwainu olungama, samala iwe onyoza chisilamu mulungu amalanga pansi pompano chifukwa cha matama ndikufuna kutchuka pazinthu za chipembedzo