E-Mail 'Mussa testifies in Chaponda case, says Malawi ruling party operates a decentralized policy : ‘Money could be for DPP’' To A Friend

Email a copy of 'Mussa testifies in Chaponda case, says Malawi ruling party operates a decentralized policy : ‘Money could be for DPP’' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
newest oldest most voted
Notify of
Adada
Guest
Adada

Ahaha.. Malawians eish! tione media tsopano.. odziwa chilungamo ndi ambuye ,even my position on this whole issue ambuye akuidziwa but amapangatu expose ntahwi inayake hmmm

Gwamula
Guest
Gwamula

ACB mukuyenela kuthinitsa khwekhwe wanu. Apa Mussa ndi Dausi alekana zokamba with intent to create a conflict in the evidence hence a doubt in Chaponda’s favour.
Chikhala ine nkadati tifufuze mmene chipani chichitila ndimakobili awo; kodi alidi ndima separate regional accounts?; kodi regional treasurer ali ndima notes opelekela ndalama kwa aChaponda mmene anachita ma fundraising awo; ndipo pali umboni wanji womwe analandilila ndalamazi?; committee ya region ifufuzidwe komaso a treasurer ndi organizing team yawo zifotokoze. Apapa muliyenela kuchita kafukufuku woonjezela.
Komabe kuyankhula kwa a Mussa ndimaganizi awo chabe. Kodi ndimmene adalembetsela statement yawo yaumboni panthawi yofufuzidwa?
Ntchito iyo

Mwana Chaponda
Guest
Mwana Chaponda

Komatu apapa Henry Mussa wayeletsa anthu mmaso.Amafuna akane. heheheheheheheh

Mwana Mulanje
Guest
Mwana Mulanje

There is nothing surprising.Isn’t Chaponda the Veep for DPP? Zikanakhala zodabwitsa zikanakhala ndi munthu ngati a Dausi

Angel Onani
Guest
Angel Onani

George Chaponda will soon be a free man.God is good all the time

Somani K
Guest
Somani K

Eeee koma we all tried to crucify Chaponda koma eee.What if we are all wrong? what if he was framed?

Gitta
Guest
Gitta

Whoever crafted this and framed Chaponda is now feeling stupid.Back to square one.

Connie in UK
Guest
Connie in UK

George Chaponda is a survivor!

Evans Jambawe
Guest
Evans Jambawe

Gmae tembenu.Watsala Goodal Gondwe to testify.Wina amwa tameki! ndithu wina amwa tameki!

Rudo Chakwera
Guest
Rudo Chakwera

Malawians lets not waste time with nsanje.We can’t all be politicians. One President at a time.