Email a copy of 'Mutharika behaving like ‘dictator’ - Church and Society' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

111 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MaKopa
MaKopa
8 years ago

This man is dictator watch this space—-??¿?¿?¿??

true
true
8 years ago

Iwe wa sutsana ndi a Livingstonia walephera kumvetsa zomwe alivinstonia amathandauza,komanso nkhani yomwe wakamba ya chipani chaku mpoto,Afford,ndi nkhani yomwe peter mtalika anachita iye monga mtsogoleri si zikugwirizana,Peter bolanso bingu iwe sunaone?bingu anayamba dictator second term,koma peter wayamba dictatorship chaka chomwecho.Kodi iwe wekha mabvuto awa akuchitika ndi peter kungoyamba chaka sunaoni?boma lake satenga anamwino,aphunzitsi,kukwenza xool fees,kuyambitsa fees ku TTC,kwacha kugwa tsiku ndi tsiku.Boma maudindo onse 3 kotaz mtundu wake wa lomwe.Ukhale pomwepo uwone pomwe malawi abvutikile ngati Ambuye satiyankha kuti zinthu zinsinthe.

eneah kaunda
eneah kaunda
8 years ago

Nafenso tisamale mayankhulidwe athu. vuto lakuno ku malawi atsogoleri timawonerera kwambiri.

nkhakamila
nkhakamila
8 years ago

mulibe mtsogoleri mmalawi….enanu kukupasani dziko kuti muyendetse nde zikhala worse.malawians need deliverance..
i dont see a visionary leader in malawi…not even Chakwera……

nkhakamila
nkhakamila
8 years ago

livingstonia synod..i think its high time you have stayed without a strong political party in the north.you boost that you are educated but how are you going to enter the government without a party.i sometimes feel sorry for u because you are selfish even amongst yourselves.you fail to support each other politically..you fail to solve small issues like that of Rev Chimwemwe Mhango our visionary pastor.you allowed the once only strong party in the north AFORD to die and later ended up to be chipani cha mlamu mchimwene and alongosi.lack of ambition.i admire UDF and DPP. if you know maths..calculate… Read more »

The Patriot
The Patriot
8 years ago

More fire, CSO and Livingstonia synod! After an emotional speech punctuated by banging of tables what next? History repeats itself! ALhhomwe, dont behave as if Malawi will always be ruled by a Lhomwe, very soon it will be under a non Lhomwe, tidzaone kuti Nophiya wanu adzayenda bwanji! Muyambilanso ma drama monga kale, pano simukutamika?

Zuwayo
Zuwayo
8 years ago

Mavuto aliko lerowa nthawi ya amai analiko koma ndi mtumbuka uti amayankhula, ndi agalu omwewa amayankhula come to Local government amene asali wampoto no allowance, agalu inu atumbuka..kuthamangitsa DC ku karonga chifukwa chakuti ndi waku Dowa, anthu omwe akugwira ntchito ku mpoto omwe si atumbuka ndi muhesha.mabungwe awa amakana kulemba achewa ntchito.FICA FAO, LAnd O Lakes, BP malawi, mzuzu coffee. Mzuzu city, heifer, total malawi, pano akufuna kuchotsesa ntchito achewa ku local government, plan malawi, mzuzu university, toyota malawi etc

Davidmakiyi
Davidmakiyi
8 years ago

mukamakwikwiya ndiye kuti mukulakwitsadi ife tinathawa umphawi kodi simunauthetsebe Abingu, Ndiye bola akadalamulira abusa aja……

Alfred
8 years ago

Musalire lero mudachita kumuvotera koma mukudziwatu.

George Kamanga
George Kamanga
8 years ago

Ulamuliro ochita kubera zimatero

Read previous post:
Karonga DC defiantly returns to work: Malawi Police arrest striking council workers

Drama continues at Karonga District Council between the workers and the embattled District Commissioner Rosemary Moyo as the DC has...

Close