Email a copy of 'Mutharika hits at ‘fwee, fwee fault finders’, says early Xmas party for children not funded by Malawi govt' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika hits at ‘fwee, fwee fault finders’, says early Xmas party for children not funded by Malawi govt' to a friend
They say music is power, yes and as proved, state owned Malawi Broadcasting Corporation Television (MBC TV) has purportedly banned...
Mwatiwoonjeza a opposition wakutoperani munthu wamkulu kkkkk
Wachimwa
Mwanyanya a Malawi or ine nditha kuluza temper, chilungamo chikusowa ife a Malawi
Ine ngakhale mdzuklu wanga sindingamutulutsile mau oterowo, mpaka fwee fwee fwee pulezident watunthu? Ai zochititsa manyazi, nkhani yake itiyo yotukwanilayo? Mukujaila kwambili ndithu, abale anu aja ankaticha tankhwenzule,tinkhuku lero inu mwayamba yanu chaka chosatha mkomwe. Palibenso chikusonyeza kuti kuli pulezidenti mu Malawi muno mudziwika mkutukwanako basi.
Mwaenjeza a Pitala mpaka fwee fwee fwee pamaso pa ana?
GATI PITALA AKUTI AMALAWI NDI FWEE FWEEE IYENSO FWEEE FWEEE FWEEE FWEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEE KKKKKKKKKKKKKKKKKKK FWEE FWEE WOYE!!!!!!!!!!!!!
President wotukana pamaso pa ana ang’oang’ono ngati uyu sindinamuone, may be he had one two glasses of whisky. Does this portray a good image of a president to the kids who went to state house, sianawonso pano angoti ndisakumve ukuti fwee fwee wamva.
We had Mr. Fotseki who is now a bed fellow to Peter and now we have a Mr. fwee fwee. Since they are now buddies the political engineer might have panel beaten him to start using a bit of vulgar language.
Zankhutu uyu ndiye mmati pulezidenti?? Ndiye pulezidenti wa kaliati ndi kaphaletu nanga wamalawi??? Uuu ine ndekha ayi nothing presidential here
APM do not bragg about having funded the party from your own pocket even though I doubt very much if that’s the case considering you are known to use our tax money and tell us it was from well wishers. If you don’t mind sharing who were the well wishers that funded the party? NAC or RBM? you are a failed president APM I do hope the prostate cancer will take you sooner than later as you are a disgrace to our nation.
Bola anawo akadzakhala mapresident asadzakhale ngati inu bwana.
Kodi K36.8million mwaonga paphwandolo simukanatha kugulako mankhwala?
Ndiye kuti inunso bwana nthawi ija munkamulangiza JB munkachita FWE FWE FWE FWE FWE?
Hahahahahahahahaha!