Email a copy of 'Mutharika installs Ngolongoliwa as Paramount Chief of the Lhomwe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika installs Ngolongoliwa as Paramount Chief of the Lhomwe' to a friend
Silver Strikers FC set up an Airtel Top 8 final clash against Mighty Be Forward Wanderers after outwitting Kamuzu Barracks...
Ngongole wa performs rituals for APM. Ndi sing’anga wa a president.
From a village head to Paramount Chief two years later? He must be ruling his subjects with the genius of the Einstein calibre or a good boy or very close to the powers that be.
Paramount chieftaincy snatched from somewhere in Phalombe?
We need to be very careful otherwise ten years to come will have more than 50 paramount chiefs in Malawi……..zandale izii……uyu ali royal to the ruling DPP….Chikadzalowa chipani china,,,,paramount-yu akadzachita mwano tidzaphwetsa mpaka adzafika pa GVH
Zabwino zonse Malume anga.Pompano paramount ayii anzathu zikuyenda.God bless u
Some 2 years ago, uyu mukuti ngongoliwa uyu was a mere village headman, pano mukuti paramount!!!! In the next 2 years afika pa prophet or pope tu
Akuti akhala emperor in 2019. Za ziii
ma rituals sizacilendo mamunayi
Congratulations for the new mfumu Juma.
Ufumu olanda a Nkhumba kamba koti a Ngibfoliwa amakachita ma rituals pa mtumbira heheeee
Atcheya kumeneko ndiye kukhala wamkulu azioneka. Nthawi yaitali Atcheya mwakhala mukunena kuti pena paliponse tidzikhalirana limodzi. Well done chair.
Am happy to have lhomwe paramount Chief may almighty God guide our paramount akhale ndi moyo wautali Tibwera tidzadye nawo mbewa viva Ngolongoliwa wohakalhalha pwiyaaaaaaaaaa