Email a copy of 'Mutharika issues certificates to DPP parliamentary candidates' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
jogoda
jogoda
5 years ago

asiyeni anthuwa. afuna kugwada okha. its not a rule. maybe its a malawian style that we are used . even kwa anfumu timagwada paja tonse musaiwaletu

Shuja
5 years ago

Moti inuyo atakuitanani a president muntha kuimilila akukupasani zinthu olo mukungolankhula nawo poti olo Dr chakwela antha kugwada

Yaphama
Yaphama
5 years ago

Kkkkkkk!! Asaaa mpaka kugwaditsana cz of paper zilipo mpaka lero zomvetsa chisoni ndi manyanzi

Sato
Sato
5 years ago

Koma mwati a Pulofesa samachita ma drama ku Amerika analiko chifukwa sabata IMENEYI ndiye aakita sizinaonekenso.

Mangochi kabwafu
Mangochi kabwafu
5 years ago

Certificate, kikikikikiiiii. Come May, paulendo.

Njolo mpilu
Njolo mpilu
5 years ago

Kodi kukanika kugwada!!!!
Obesity in malawi nde yayayaya
Amati ndi kudya bwino osati killing self slowly.
Mimba ngati zikwatu, zopanda shape
Zina ngati timikhate
Zina ngati akulunga vinsalu kutsogoloku
Ma bobrov
They all look ugly arses.
Ngati ndi style bola kumeta mipala kwinako ukucotsa maonekedwe atsitsi la matenda.
Cifukwa nde olo kuti mw is one of the poorest trading centre.

chakwana chakwana
chakwana chakwana
5 years ago

this is too much mpaka kugwaditsana? May be azimayi koma men? mmmmmmmm ukapolo ulipo ku DPP ndithu

Hhhg
Hhhg
5 years ago

APM: Aaah nonse olephera kupeza mpando umeneu Wa u chimulirenji uwu,ahh phephaani kambrrr

Onse: AI sitimaufuna bwana

APM: Tchoontchooo nzokondweesa kwambrrr

APM: Tchabwino,nonse ndandanindandani apha ndikuphaseni ma satfket

Chief Obasanjo
5 years ago

Why kneeling, you people sure this time.

Mangochi kabwafu
Mangochi kabwafu
5 years ago
Reply to  Chief Obasanjo

That’s how you realise how stupid these ideots are.

Mangochi kabwafu
Mangochi kabwafu
5 years ago
Reply to  Chief Obasanjo

That’s how you realise how stupid these idiots are.

Truth Pains
5 years ago

Kkkkk koma zinadzi mpaka a Nankhumwa kukanika kugwada chifukwa chonenepa miyendo.

Agogo a Goodall anagwada bwanji??? Am just curious to know his pose,

Time is up for DPP, let’s wait and see .

Read previous post:
Joyce Banda set to raise Malawi minimum wage by 64%: Pledges to create smart villages

Former president Joyce Banda says her administration will raise the minimum wage for all Malawian employees to K40 000 from...

Close