Email a copy of 'Mutharika jail cell visit ‘stinks’ – Mayaya' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika jail cell visit ‘stinks’ – Mayaya' to a friend
Mighty Be Forward Wanderers new catch from Big Bullets Jimmy 'Ginola' Zakazaka was in top form on Wednesday as he...
uyu ndiyo kaya. Izi amapanga ndi ana Ku primary kulemba mu ma toilet ndi bibi
Taking graffiti to another level… That is exactly what we are teaching Malawians
kkkkkkkkkkkkkkkk! kulila mokweza a Mayaya. Pangani zanu. asiyeni anzanu ndi nthawi yawo. za ziiiiiii! kapenteni nau ndende. poti munalemba mmadzi a PP chule anafuta. mumayesa akaferamo kkkkkkkkkkkkkkk! wangosiyamo signature tu basi!
I dont trust our POLICE , police is there for the entire country…….Apolice alola bwanji kuti anthuwa akalowe mkulemba pakhoma ? Police statation yomwe ikugwiritsidwabe ntchito… yomwe sinakhale miziyamu? apa akuwonetsa mbali apolice kuti amasopota DPP..
MKATI MWAKE KU PENTEDWA BLUE…….AAAH NO MALAWIANS…. I WISH APOLICE AKADAMAGWIRA NTCHITO MOSAWOPA MUNTHU… if it was like me to write on that that wall apolice sakadalola or half…cell ya 3days aaaaaaah.
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Iwe ‘Aferazao’ ndiwe chitsiru kwabasi. How do u compare this sheet with sugar cane sellers from Nambuma? Unamva kwa ndani kuti anthu a ku Nambuma amaganiza mopepera. Ndiye chitsiru ku Nambuma kulibe a Lomwe wamva. Only Lomwe behave in disgusting ways osasokoneza zinthu. Kugulitsa mizimbe ndi kulakwa? Fotseki
Very bad acts indeed! How. Can the whole of the state president do such a thing. Totally impossible
Nyapapi
hahahaha, , , , , ,koma guys
This guy likes graffiti on walls, etc. You will remember he also cut his name and Bingu’s on a tree in his home village. The tree still stands with its tattoos today. If we dont stop him, he will write his name on everything he sees. Watch out Sanjika, Presidential Palace, Ndata, shortly he wants his name written on the hills and mountains of Malawi.