Email a copy of 'Mutharika meets Malawi Law Society over judiciary impasse' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika meets Malawi Law Society over judiciary impasse' to a friend
Children who were hosted by Malawi President Peter Mutharika and the First Lady Gertrude Mutharika to a Christmas Party at Kamuzu Palace, in the...
careful achina Felisah. Mambulasa ndi wa DPP. Make sure yammanja yanu wakupatsani yokwanira otherwise akupondani. Anali a Born Again kale, a Chairman a Chanco Church. Koma pano DPP inaalowa mmagazi anataya Mulungu.
Alandira anganene maloya ndi mbanvanso.
Kunalibe za mmanja kumeneko?
Mambulasa, Powell, Felisah, Gibo, Jamzy… and a senior citizen. Ma lawyer a pa Malawi.
5 out of the 6 lawyers ndi achinyamata. Nanga bambo awowo achi 6’wo ndi atchuwa? Akalamba nazo.
Sorry Malawi
Majamanda wangonenepa nkhope yokha. Koma timiyendo ngati nsungwi how?
Kodi anzanganu , tell me more about this boy , Ben Phiri? Kodi ndi uja amadyamo abwana uja? Akuti Ali ndi nsete zokoma kwambiri? Zomwe winayo samafuna kutalikila Nazo?
Kkk a malawi amenewo you are talking but failing on death ear. Poor people have no voice.
A Ben Kuyima ngati akufuna kujowa uli ulemu pa photo