Email a copy of 'Mutharika outlines major developments for Kasungu' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

21 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
ndatopa
ndatopa
5 years ago

you only have 6 months left where have you been???

mediaz
mediaz
5 years ago

Week yino tidamva kuti Ku kasungu anthu athamangitsa ogwira ntchito Ku unduna zamalimidwe pankhani ya ma coupon.Mwayiwala kale nthawi yomweyi?Penapake amalawi muli ndi vuto kumangowombera mmanja chilichonse,adakudyetsani chani?Uchitsiruwu muzaleka liti?Ku phalombe pitala wanuyo akulephera kumanga chipatala,Ku Blantyre akulephera kumangakumanga kumanga police yanuwani,ndiye kukasunguko kwapambana panji?Galamukani a Malawi heeeee!!

Chilungamo
Chilungamo
5 years ago

Kodi convoy iyo imayenda museu wake uti? Wa Lumbadzi-Mponela-Chikhoma- Kasungu? Osapanga manyazi?
Kodi chitukuko ‘cho, why didn’t this road get priority this past 5 year? We are talking of M-1 Road here, a National Road, the face of the country.
But this DPP government is a joke!!!

Noxy
5 years ago

DPP is still very hot! Chitukuko chimayankhula kuposa pakamwa .

Napoleon muza
5 years ago

Shaaah, wins achita kamwazi ndithu. People of Kasungu knows how DPP government respected their own son, Dr H Kamuzu Banda. Who can forget that in Kasungu. There are little things that matters most to people in life. Bythewaywhich party is not ferrying people to its meeting. I even know disputes that are going on in MCP primaries because of candidates ferrying people.

Mose
Mose
5 years ago

Mukufuna kuwanamiza anthu aku Kasungu kachikena eeeh koma anthu andale ndinu olimba mtima

Achalume
Achalume
5 years ago

zayambaso liti izi zomakwera pa campaigning vehicle ndiakazanu heheheehe

Wiseman
Wiseman
5 years ago
Reply to  Achalume

Pali vuto lanji apa? Kungofuna kupeza vuto paliponse, amalawi khalidwe loyipa kwambiri. Ndikulakwa kuyenda ndi mkazi wako?

mmc
mmc
5 years ago

Ku South zitukoko zake ziti? Pa nkhani ya Chitukoko DPP shares equally. Koma kungoti the pace we do these so called developments is not ok. Likakhala tsankho ilo ndi vuto la a Malawi tonse. The north tsankho..centre tsankho…south tsankho.. we need to learn to live well together as one..

danielle
5 years ago

president of empty promises, you promised to reduce presidential powers, six universities, independence of ACB, lake Malawi boundary with Tanzania etc……. any progress on these? u pack up and go!!

linda
5 years ago

ma university six munalonjeza 2014 aja ali kuti? Nanga Nsanje inland port waisekula? empty promises, clueless, useless president…………..

Read previous post:
Malawi govt lines up 10 bills for Parliament: CSOs want MPs to summon Mutharika 

Government has lined up 10 bills for debate in the forthcoming seating of parliament which starts Monday but officials from...

Close