Email a copy of 'Mutharika to participate in anti-albino killings march' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika to participate in anti-albino killings march' to a friend
Officials of the Karonga district council have suspended a Director of Finance (DOF) Sanderson Nyirenda with an immediate effect after...
Kikikkkk kubisala kumeneko?
Muthalika does not need to match but act. If he is clueless on what he can do, let me tip him: Tell the Minister of home affairs, the police IG, the Police Commisioners from each region, the Officer Incharges from all Districts, the Station Officers from each polite station, the heads of police units, TAs, GVHs and Village heads this clear message: “ONE MORE KILLING OF AN ALBINO IN YOUR AREA OF JURISDICTION, YOU ARE FIRED BECAUSE YOU HAVE NOT UPHELD THE RIGHT TO LIFE OF A HUMAN BEING. BESIDES YOU WILL ANSWER ADMINISTRATIVE CHARGES OF NEGLIGENCY.” THIS MESSAGE WILL… Read more »
President wanji omapita ku demonstration. Izi ndi zimene Malopa akumuzuzula nazo Kalinde kuti munthu wapampando asamataye nthawi ndi kumakayenda panseu mmalo moti apeze njira zoti malamulo agwire bwino ntchito. A president athu, mukuyenda panseu kuti mutani? Mmayesa inu mukanachita mphamvu apolisi akhale akuyenda mmuzimu, komanso ma young cadet auzidwe kuti ateteze ma alubino.
SPEECHLESS NOW ON THESE CASES…..MARCHING DOESNT ADD ANY VALUE
akukamuyendera ndani? Ife tikukayenda kuti asayine death sentence. Iyeyo akukayenda kuti chani? What does he want and from who?
Akayenda mbundalanda? Asakagwetu katundu yense pamtunda