Email a copy of 'Mutharika returns this weekend from New York' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika returns this weekend from New York' to a friend
A cattle rustler in Chikwawa Mike Sintidu - a well known butcher in the district- has been handed a five-year- jail sentence ...
Whether he comes back over the weekend or next year in May just before the elections is neither here nor there. Malawian won’t miss him anyway. However, he will likely be voted in whether he is here or in the US. Says a lot about Malawian voters.
Koma ine ndilibe naye ntchito m’dala ameneyu. Kaya abwera kaya sabwera koma ndi one tinathana kalekale. He’s just a useless man
Azimayi a dpp, odi ukoooo!! Kpnzekani sambani, Maliseche akubwera muzikavina nawoooo
He’s still in US wasting taco money while the country begs for aid from
melania to fix broken schools. You pet are indeed a sit holes country
Thank yoU Melania Trump for cutting Mr and Mrs Maliseche’s trip short, you just saved us a lot of Tax payers money,
Join the discussion…Kkkkkkkkkkkk pitala
Is it just my observation that for the past UNGA no single African head of state has made impact on the stage worth BBC , Al Jazeera or CNN mention. It seems their speeches are so lukewarm and uninspiring that no one takes notice. In fact these African leaders are so ineffective at their own regional body AU that no one in Africa is interested.
It’s just a big boys club, nothing to write home about it’s a serious waste of resources
No need to return to Malawi Mr President, you being here makes very little impact. Mchacha and his brigade of cadets are running the show with or without you.
total shame. the whole educated minister wearing colours of a political party in AMERICA. as if she is in mponela near kasangadzi river. my foot
…thus what we call loyalty
2017 there was not a single fatal air accident in the whole world. So far 200 plus have died this year. Just statistics sindikunena kuti awanso ndege yao igwe. Koma zitatero mwina Malawi tingapulumuke mu gehena tili lero. May kwatalika amalawi tili pa moto ndalama akuseweretsa akuluwa mapwevupwevu
Inu ndinu achitsiru othelatu,how can a normal person wish his leader death?….muzipita ku Zomba basi
Not only his leader but his fellow human being. Amalawi nsanje yanu yafika potero mpaka? Mwagulitsa umunthu wanu chifukwa cha ndale? Ayi ndithu patrick mbewe inensotu mfunda wanga ndi mbewe ndiye ndikukupemphani kuti muchepetse nkwiyo wanu ndithu, ukuwonongetsa chikhalidwe chanu chenicheni cha chimalawi. Ngati wachibale wanu akamwalira kaya pa ngozi kaya pa matenda, inu ndikumava chisoni ndikumalira, ndimomwemonso achibale a Peter Mutharika ndi anthu ena akwere nawo mundegewo azamvere kupweteka ngati iwo atamwalira. Ndikhulupilira thembelero mwaliika pa anthu awa silibwera mubanja lanu first, chifukwa nthawi zambiri ndimmene zimakhalira. Kukumba chidzenje kuti wina agweremo, umagweramo ndi iwe kapena okondedwa wako instead.
Kusavinidwa
MALISECHE AKUBWERAAAAAA!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Amwene umunthu mulibe and you don’t even know how serious is a plane crash ngati kuli kulodzedwa akulodzani kwambiri. Uzaziwona m’mene zimakhalira when you are involved in the situation you are now proud of.
Kumakhala serious aMalawi.
Dzenje walikumbali Patrick Mbewe ulitseka wekha. Pitala ndi anthu onse afika bwino bwino ndipo 2019 awinanso chisankho. Akakukomula mtima Mulungu udzaziona.
Wishing someone death is a total sign of immaturity