Email a copy of 'Mutharika says construction of Liwonde Bridge manifesting his development agenda' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Angoni
Angoni
5 years ago

8 more months and we will be done with this stupidity!

Dr Manga
5 years ago

The bridge is being funded by the USA under the MCA. Tisalubwelubwe apa.

#DzukaniAmalawi
#DzukaniAmalawi
5 years ago

The people of Malawi have paid K1,5 trillion in taxes so that the govt can use the funds wisely including building infrastructure. Any fool can build a bridge but takes a visionary leaders to do more with the meagre tax money for the good of generations to come.

concerned citizen
concerned citizen
5 years ago

Zosiriyana Zosiyirana, Zosiyirana.

concerned citizen
concerned citizen
5 years ago

Ndiudundo wachipani chirichonse chimene chingalowe mboma kutukula dziko. Palibe chifukwa choimbira ngoma kuti ndapanga chakuti chakuti. More over ndimisonkho yathu ife amalawi yomwe mukuchitila zitukukozo popeza tinakulembani nchito kuti muyendetse dzikoli for five years . Mukayendetsa bwino mokomela a Malawi in all areas of running government affairs, Malawians will vote for you again to run the country for another five years. Musanabwere inu anzanu achitapo mbali yao. Ndizositirana izi.

Shitholes dpp
5 years ago

The bridge started during Joyce Banda era and is donor funded. Please Alamu Pumani Mwakula don’t personalize development as if from your pocket. Sometimes people will commend you for thanking your predecessors. Musadzikundikire. Zakuba kwanu aliyense akudziwa. Mwabweza K145 million. Izi nochepa.

Dipipi wa Yudiefu
Dipipi wa Yudiefu
5 years ago
Reply to  Shitholes dpp

Akupanga chimodzimodzi ndi ma post office omanga a kongilesi ati one stop centres . Kungopenta kukhala ngati amanga ndiwowo. KuMangochi amvekere tamanga one stop centre. Kodi Pumbwa uyu akuyesa anthu kuMalawi ndiwogona kwambiri eti?

Duduzane
5 years ago

Utsogoleri wa ku malawi ndi ochitisa manyazi heavy . Ndimakhala ku George south Africa kwakhala kukumangidwa zinthu zammbiri mbiri koma sindinaonepo nduna ikubwera kuzatsegulira. Nanji President. Koma ku malawi abale ndi bridge yomwe President kusiya ntchito . Kukatsegula bridge? Musamatixhitise manyazi guys

Natty Prince
Natty Prince
5 years ago

Inu ndalama za misonkho ya wanthu izi mayiko otukuka kuulaya purezidenti sataya nthawi ndikumayendayenda kukatsegulira zili zonse iyayi mwakhala ku United Snakes of Amerika zaka zambiri koma simunaphunzire olo kuona mmene amzanu amapangira iyayi?Chlili chonse ndale komanso ndale zake zonngoziwa kuba basi ndikuputsitsa wanthu.

Read previous post:
Eastern region for DPP, says Mutharika as throusands welcome him in Mangochi

Thousands upon thousands thronged Mangochi Boma to welcome President Prof. Peter Mutharika on his whistle-stop from Blantyre to state residence,...

Close