Email a copy of 'Mutharika starts whistle-stop campaign blitz, promises 'better Malawi'' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

15 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Pension Nenereko
Pension Nenereko
6 years ago

Kuti Chikoko Bay State Lodge, kuja kudzankhale rigging centre eti?

Tsamba Likagwa
Tsamba Likagwa
6 years ago

Ayamba kale! ayamba kale? …. Ayamba kale kunjenjemerala!
Atangomva kuti Apitala alubwera apo ayamba kale kunjenjemela.

Boma ilooooooo!

Kaya wina afune asafune DPP boma
Peter Muntharika Boma 2019

Mfumujay
Mfumujay
6 years ago

Kodi telela wawo ndani?

Prof. Mathanyula
6 years ago

Za ziii, chitukuko chake katangale yemwe mukuchitayotu. Talozani zomwe mwapanga pa three years yomwe mwakhala mukuba ndalama zathu. MK577bn tikuyifuna mudzabweze after 2019 chifukwa mudzakhala kunja kwa boma ndipo simudzakhala ndi mphamvu zopondereza katangale amene uja.

Phiri
Phiri
6 years ago

Too late, too little

Citizen
Citizen
6 years ago

Kwanu kwacha inu, chaka chanu chomaliza ichi 2019 mupakira basi. You are arrogant, corrupt, nepotistic, visionless & clueless. Your late brother HE Ngwazi Prof Bingu Wa Mutharika was the best president after the late Ngwazi Dr Hastings Kamuzu Banda, Father and Founder of the Malawi Nation. May their souls rest in eternal peace! They set high standards of leadership which you are by far failing to surpass let alone match.

ANALYST
ANALYST
6 years ago

“Promising better Malawi?” I thought you are the president now and that you can make a better Malawi even now and today?? You had 3 and a half years to do that and you have the guts to promise us a “better Malawi?” Are you mad Mr President? To hell with your nonsense

Achimidzimidzi
Achimidzimidzi
6 years ago
Reply to  ANALYST

kkkkkkk!!!

Gwemula
Gwemula
6 years ago

Maimidwewo akuonetseratu kuti abwana wa ndi mbava ya corruption yaikulu ngakhale madamu wonso ngati akunena kuti zokonda amayiiii!!

psyuta
psyuta
6 years ago

Anthu ku Malawi saangapange mistake yobvotera MCP Bwana. MCP idakali ndi magazi mmanja, osaneneka.

President Manthakanjenjemereza
President Manthakanjenjemereza
6 years ago

We dont have better Malawi after ruling for 3 years why having it later.

Read previous post:
Malawi youth MPs demand stop of  ‘Lhomwelisation’ in employment and  corruption

Members of  Youth Parliament have  expressed concern in a motion the high and egregious levels of corruption and nepotism in the President Peter...

Close