Email a copy of 'Mutharika urges people of Ntcheu to continue supporting DPP and not join UTM' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika urges people of Ntcheu to continue supporting DPP and not join UTM' to a friend
Malawi Vice President Saulos Chilima has returned from Nigeria where he attended the two day Africa-Israel dialogue summit. Chilima was...
I believe ma cadet ma comment wa mukumawerenga. Please, kawaudzeni Agogo zinthu sizili bwino, chonde musamawapusitse ayi. Munthuyu ndi wabwino koma utsogoleri simbali yao ndipo muloreni gogo wathu akapume ndipo alandire ulemu ngati president wopuma. Malawi si ili ready kukhala ndi another state funeral, I am sorry koma komwe kukupita zinthuku, one can openly say kuti mdalayu mumupweteketsa – I rest my case
PRIORITIES FOR NTCHEU IN ORDER OF IMPORTANCE.
1.STADIUM
2.WATER
Don’t trust Inkosi Kwataine…..he’s Saulos Chilima’s good fvriend…..anangoyankhula as a formality. I know him quite well…
DPP inali ya BINGU osati MBAVA IWE
Nde mati tisavotere ndani? Kkk ur mad.
A bwana inu , muziti pheee muzawona nokha mumene azayakhile a Malawi, ngati ntchito zabwino zizakuchitilani umboni pa 21 may 2019.Dikilani bwana yakho likubwela pa may 21 chaka 2019
Muthalika is mad and useless. Person with no value APM
DPP INALI YA MALEMU BINGU NOT YOU
Maliseche anthu kuvomereza.
M’dala wakuba