Email a copy of 'Mutharika visists Thyolo flood victims: Govt extends social services to cater for disaster victims' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika visists Thyolo flood victims: Govt extends social services to cater for disaster victims' to a friend
A renowned Mchinji businessman based in Lilongwe, Fedeliko Chikakula allegedly committed suicide on Sunday when he by shot himself with...
Munthu monga mtsogoleri wa chipani azidziwika kuti ali kwao poonela kuchula kwa anthu. Nanga a Chakwera akapita ku Kasiya kumangokhala anthu atatu okha? Akakhala Chilima ndiye amaopa kukachititsa misonkhano kwao ku Ntcheu, kuti angakachiteko manyazi.
Ana achepa, tikunyetsani nonse. Dziwani kuti anthu amenewo onse adzavotera DPP ndi ochepa okha ozungulira mitu ngati achina Wandale omwe adzavotere zipani zinazi.
Sichipongwe koma kodi ndiye kuti madzi osefukilawo angokokolora katundu ndi zovala zonse kupatula zachipani? chifukwa ndikaonetsetsa malo onse anthu akumavala zachipani
Those are not crowds of people but of DPP followers otherwise everyone wud have been in their own clothes not everyone wearing blue
Ndipodi inu. Onse ofuna thandizo koma kuvala blue. Indeed their own supporters. Who is fooling who? Nyengo yamara. 21st May come soon soon please.