Email a copy of 'Mutharika’s step-son Tadikira in ‘vote for A Dad’ campaign amongst college-going students' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

38 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
gwenenthe mwale
gwenenthe mwale
4 years ago

tell your step father that he is very old. he doesnt care for malawians. he is dull
he doesnt perform

jjjjjjj
4 years ago

Iwe ndi adadi akowo tikulaitchani lachiwirili. Ngati mukudya bwino ndimisonkho yathu imeneyo and udziwe kuti olipirafe sikutipindulira. Only fools will vote for the so called step father of your. To hell all of you

2019 MCP BOMA
2019 MCP BOMA
4 years ago

AGOGO PETER MUTHALIKA ACHEPA,FUNDO ALIBENSO! TAWONANI LERO KU DEDZA NUKUMATCHULA PROGRAMME IYI YA NDALAMA ZA MISONKHO YA ANZATHU A KU GERMAN,EUROPEAN UNION, IRELAND YA MTUKULA PAKHOMO YOMWE YINAYAMBA MCHAKA CHA 2006 NDIKUMATI NDI YAKE ZOWONA? CHONSECHI PROGRAMME YOMWEYI YOYENDESEDWA NDI MISONKHO YATHU YIKUMUKANIKA KWAKE KU THYOLO.PROGRAME IYI YAMTUKULA PAKHOMO SIYINAYIMEPO NGAKHALE NTHAWI YA JOYCE BANDA OR PETER MUTHALIKA ATAMWALIRA LERO YIPITILILA BASI. KODI IWE MWANA WA GETRUDE A DPP NSANJE PORT AMANGA IJA ANAWALONJEZA ANTHU A KU NSANJE MU 2014? MILANDU YA MA FILE 13 A CASHGATE YA MK234 BILLION IJA ILI PATI? INVESTIGATION YA ACB DIRECTOR WA ADMINISTRATION UJA,… Read more »

pheza
pheza
4 years ago

Mwana iwe ukakhala pofewa usaganize tonse zilichoncho kuselikuno zinthu sizilibweno

VYOTO
VYOTO
4 years ago

At 80 years old, Peter has proved to be tired in his head already, what more when he will be 83,84.choosing a very dull looking running mate in the name of Chimulirenji out of the so many capable DPP Members are clear indicators of someone who got tired sometime ago. When Professor Peter Muthalika talks, he reminds me one of my late old grandfathers whom at 80 had no single teeth in his mouth and you could hardly get anything from him and Peter wants to continue to be president for the 17 million of us? Really? It is a… Read more »

Innoxy
Innoxy
4 years ago

Chonde mbuye wanga, dzamutengeni peter mutharika kuti anthu achi-alobino apeze mtendere nawo.

Kapado Chimuthawirenji

Kodi amenyi anapambana zenizeni kuti apite ku koleji kapena anapita ku koleji chikwawa choti makolo ake ali ku m’mphika.

jjjjjjj
4 years ago

Zokaikitsa kuti anakhoza ameneyu, khalangati ndi zija amati ”it has pleased the president to send my step son to college”

Central
Central
4 years ago

Campaign ya u president wa chipani mwayamba kupanga delegate ana anu? Ooooooooooooooooooooo! Nankhumwa wamvaaaaaaaaaaa? Pali nkhanitu apaaaaaaaaaaaaaaa!

Maunits
Maunits
4 years ago

5years yapitayi ndichani cholozeka choti ife tingamvotere uzinamiza alhomwe ovotera mtunduwo ife ayi nono

mwe
mwe
4 years ago

This so called Tadikira is fond of dishing free monies around to buy popularity, recognition and acceptance. I would not be surprised that the majority of the youth at this gathering are after his reckless spending as opposed to supporting APM. No wise student who wants a bright future would vote for APM. Guys eat the money he has brought there after all the money Is our taxes though badly spent . Tadikira as a step son of APM will be a nobody soon when the taps close and he does not have access to fake supply contracts of medicines… Read more »

Read previous post:
Kamuzu Day: Malawi remembers ruthless dictator who caused a lot of pain to many people 

Ngwazi Dr Hastings Kamuzu Banda  clearly loved Malawi as a country. He took advantage of generous development aid projects of...

Close