Email a copy of 'Mvula to join Malawi FA presidential race: Nyamilandu’s 4th term bid faces more challengers' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

25 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
The Swartkop Guru
The Swartkop Guru
8 years ago

Malawian are really a strange people. I now believe this! Kodi what’s a problem with Humphrey Mvula? Sanathese Shire Bus Lines… The guy was fired and iy was from there when People failed to Manage the Busliner.

People forget now that it was Mvula who brought the luxury buses to Malawi… You remember Sacramento and Paradiso?

Ufiti basi a Malawi… Kusatukuta. Mumadziwa chani agulu inu…. Mumavota ndinu? Tamangotuwani ndi umphawi..

Mvula go Mvula go

maruwasa
maruwasa
8 years ago

A Mvula afuna akabetu basi stupid mafia galu iwe

Thom Paul Duncan Nkalodzwa

Humphrey C. Mvula the mafia and politician. Destroyer of BUS company kk Koma Yeaaaaa, dyera likakula limasauka ndi dziko

Ng'ombeyavuka
Ng'ombeyavuka
8 years ago

Mvula mwene yuyu basi, stage coach and FAM vithu viwili vakupambana.we want brains to lead FAM like him. Mvula more fire!!!!!!

alpha
alpha
8 years ago

ngati ndatukwana pepani.The issue is chi Walter palibe chimene chachita zaka zonsenzi, so the playboy MUST GO.
Anthu alipo koma chabe tsegulani maso. Walter amakuopysani ndi chiyani?

alpha
alpha
8 years ago

Agree,. No Walter and no Mvula. Walter wangokula mawu koma galu wa munthu sadziwa kuyendetsa mpira. Kukakamira udindo zaonetsa kuti ichi ndi tserekwete cha munthu.

Mvula vuto koma ufiti.. Komanso anathetsa basi yolimba phuu! can you imagine what the guy can be able to manage? a Malawi pepani. Tsegulani maso anthu alipo.

A Nyirenda, tamatukukani mungomva kuti ndinu a ku mpoto. basi mwati ine koma u vice?
Try FAM presidency. Ndinu nokha mumadziwa mpira komanso mumakamba za mzeru. enawa amatisandzitsa.

wabullets
wabullets
8 years ago

munagwetsa shire bus co. nde mufuna mukagwetse fam,,,,, usawi chichi?

Tamanda SaukaK
Tamanda SaukaK
8 years ago

Kodi a Mvula asiya ndale. Back from retirement. Koma yeaaa. Kodi salary ndi bwanji? And what are the benefits? Ife anyerere pambuyo panu nga nga nga

jaman
8 years ago

mpaka zafika pa mvula he he he he he agogo asiireni achinyamata zinthuzi water yo nso sakufunika tatopa naye

waziona
8 years ago

Both nyamilandu and mvula are not wanted to manage football in malawi

Read previous post:
Silver plot Bullets raid when transfer window opens

Silver Strikers  are hoping to bolster their squad with the double signing of champions Big Bullets pair rejuvenated striker Chiukepo Msowoya...

Close