Email a copy of 'Mwanamvekha joins race for DPP veep post: Malawi ruling party convention gets exciting' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mwanamvekha joins race for DPP veep post: Malawi ruling party convention gets exciting' to a friend
Silver Strikers have climbed to the summit of the TNM Super League for the first time this season following a...
Ok
The article couldn’t say it any better, he is a hard worker and we need more people like him in this country
Ndye vuto la dyera’lo. Muyamba kulumana, kuphana nokhakha MILHAKHO tsono. Kondwani akuti koma ine, Chapondachimanga sakulora akuti a president mungonditsakha, wina akuti ine CV & track record yanga is impeccable.
It’s all GREED, INSATIABLE APPETITE!!! Nyenyanani, lumanani, dyanani nokhanokha. Mumaona ngati zidzathera kuma tribes or ma region ena? Atumbuka/ Achewa/ Asena?
SHAME on MBAVA!!!
Good move…o hope it works out for him…he’s truly proven to have the interest of the country at heart
I could vote for Honourable Mwanamvekha, ntchito zawo zikuchitira umboni ndimuthu olimbikira pa ntchito iliyonse, osavera zathu. Let’s vote for someone we can trust and he will do miracles in our country
Mwanamvekha Is the best for this position.
We need people like him for Malawi to develop osati mbava zinazi.
Paja Amalawi sachedwa kuyiwala.Indepence Celebration Committee yopangidwa Chair ndi akuluwa inaphesa Ana Ku Bingu Stadium.Ati anthu Asalowe mu Stadium mpaka 10 koloko kusungira Malo ma Supporter a DPP. We have better people like Henry Mussa sanyoza munthu.Wakhala akupanga Chair ma National Celebrations koma did not make such silly blunders.We are still waiting. Kodi analamula kuti Mageti atsatsekulidwe ndani?Public Officers must always be held accountable for their decisions/actions if we are to Progress as a nation.
Good team leader…….osati ma educated savages ena awa mbuli za Chuma osavela chisoni amalawi……..mwanaveka yemweyo basi
Mwanaveka……game changer even your fellow ministers knw ur a hard worker no wonder a Jeff anati mumangotukula ku dela lanu lokha atengelepo chisanzo people elect us so that we can transform their lives not the other way around……continue the good work in your constituency and elected office of the government