Email a copy of 'Mzuzu Cops to fight against imprisonment over cell death' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mzuzu Cops to fight against imprisonment over cell death' to a friend
As Malawi TNM Super League nears the end and enters week 24, 420 goals have been scored from 170 games...
OOH yes, the truth may wonder away but it will always comeback, a strong man cannot go just like that, can yu imagine the pain he was going thru during the whole ordeal,? LORD have mercy, nawoso afe ndithu i rest my case.
let them face the big hand of law, chilungamo sichamatama, sichifuna kutchena, ruther loves to be naked, mungachiphimbe bwanji one day it will come out.
Let them face it, don,t hesitate.
Imagine if it was you Child, Imagine the pain his parents are having right now, even sending them to prison, will not bring him back, I pray for my poor country
Zoopsa,,let justice 4
Primitive tactics.Savagerly cruelty brutish. May the authorities investigate this in all the Police cells throughout the country. It could hv bn understood if he had commited murder or rape. One day you have to give an account to God
anthu awo alangidwe. apolice atatuwo ndi ankhanza kwambiri. alangidwe amangidwe basi. mwazi wa munthu wu londole justice!
Amenewa atatuwa asachedwese boma ayi koma akalowe kuti akaliziwe dziko,akaone a satana eni eni a ku prison.
Ma comment anu adzikhala athandauzo, osangoyakhula kuti wina anditame.
Police or murderers. Hang them
apolisi amalanga anthu ena pamene iwowo ndiye oipitsitsa. Akagwira chamba sanena kumene akachiyika, a traffic ndiye sheee! ma prosecutor amamanga olakwiridwa ndikumasula opalamula mlandu.
Shida Msiska anali wapolisi kukaronga Lero akuseva kumzimba prison nkhani zake ngati zomwezi. Awanso akaseve, anthu woyipa awa